Pabwalo Comedy Series

Call Directions

Pabwalo Comedy Series PABWALO COMEDY SERIES 🎭
Is based on real life β€”
what is happening in our areas,
what people go through every day,
and the experiences we all understand.

We use humor to teach, advise, and open eyes,
because laughter is better when it has meaning.

06/09/2026

Left Right!!!!

Left Right!!!!!

Yes sir!!!!!!!!
πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚
Onelani Pabwalo comedy series Season 5 EP 11 Link mu comment section

06/09/2026

Monga Buligadiya General kupangisa Training Anyamata πŸ€£πŸ˜‚πŸ˜‚

Episode 11 Yatuluka tiyeni ku YouTube,

Link mu comment section

06/09/2026

Munyeliwa wakwapula anebawudu onse ati chibaloπŸ˜‚πŸ˜‚

Episode 11 tiyeni ku YouTube
Link mu comment section

05/09/2026

Kwa Aliyese yemwe Ali ndi Luso lopanga Comedy ndipo amafunisisa atapanga Join Pabwalo Comedy Team,,,,

UTHENGA WANU UWU:

Ife a Pabwalo comedy series tilibe Sponsorship iliyose ndichifukwa Nthawi zonse mumangoona Nkhope zomwezo mwezo awa ndi okhawo omwe amangopanga Acting Chifukwa amakonda luso lawo osati ndlama,,

Nde ngati mulipo ma Artist around Blantyre komanso oti mukhoza kukwanitsa kufika ku Machinjiri kwa Chikapa,,, Yankhulani ndi Nkulu oyendesa ntchito za Pabwalo pa number iyi

+265 989 427 758

Whatsap or Call

Mwai uwu ulipo mpaka pa 07-09-2026

Shooting yayenda bwino,,,Tikumane mawa 8am Episode 11
05/09/2026

Shooting yayenda bwino,,,

Tikumane mawa 8am

Episode 11

Mukuganiza kuti apa Panali nkhani zanji???Kumbukilani mawa ndi Lojambula Pabwalo tiyeni omwe muli free tikakhale limodzi...
04/09/2026

Mukuganiza kuti apa Panali nkhani zanji???

Kumbukilani mawa ndi Lojambula Pabwalo tiyeni omwe muli free tikakhale limodzi pabwalo

Mutakumanq ndi anthu awa mungawauze mau otani??AmfumuMai MakwinjaAndunaMofati
04/09/2026

Mutakumanq ndi anthu awa mungawauze mau otani??

Amfumu
Mai Makwinja
Anduna
Mofati

Tiguleni Ma Ticket,,,Show iyi Silvester Kalizang'oma akalakatula Live ,,,,Nayo Pabwalo comedy series pambalipa ikupanga ...
03/09/2026

Tiguleni Ma Ticket,,,Show iyi Silvester Kalizang'oma akalakatula Live ,,,,Nayo Pabwalo comedy series pambalipa ikupanga zake zija Live,

Onani pa poster Po ma numbers gulani ticket

03/09/2026

Litata ndi Chibwibwi ndizosiyana,,Asing'anga pewani kunamiza anthu,,
Pabwalo timaphunzitsa!!!!!!

Episode 10 Ili ku YouTube tiyeni Link pamsipo

02/09/2026

Ayona Zipitani!!!!
Ayona Nyamukani!!!

Episode 10 Yatuluka tiyeni ku YouTube Link mu Comment section

Address

251 Pearl Street Ladium
Pretoria
0037

Telephone

+265989427758

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pabwalo Comedy Series posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category