Nkhotakota Entertainment

Nkhotakota Entertainment Promoting Nkhotakota’s music, culture, and news. We spotlight local artists, share traditions, and keep communities informed.

Our vision is to unite people through creativity, build pride in heritage, and put Nkhotakota on the map. We are a dynamic digital platform dedicated to showcasing and promoting the rich musical talent and cultural creativity from Nkhotakota, Malawi. Born from the passion to uplift local artists and connect them with fans across the globe, our mission is simple:
To be the heartbeat of Nkhotakota’s

music scene. Whether you’re a rising artist looking to promote your first single, a DJ searching for fresh vibes, or a fan wanting to vibe to homegrown sounds — this is your space.

19/08/2026

Sim'mene Kuliri Ku Lilongwe Scorchers

19/08/2026

kwachema ku KIA Ma Scorchers

Zoopsatuu KwambiriMai wina wa zaka 28, a Atness Thom wacheka kumalo obisika mai nzake atamupeza akugonana(Gagaga Dedede)...
19/08/2026

Zoopsatuu Kwambiri
Mai wina wa zaka 28, a Atness Thom wacheka kumalo obisika mai nzake atamupeza akugonana(Gagaga Dedede) ndi mamuna wake ku munda m'dera la Kapichi ku Monkey Bay.

[From inbox 📥] Hello Nkhotakota Entertainment! Ndimati mundithandizireko kusaka customer wachangu andigule REDMI A3 ndik...
18/08/2026

[From inbox 📥] Hello Nkhotakota Entertainment! Ndimati mundithandizireko kusaka customer wachangu andigule REDMI A3 ndikumutaitsa pa 270K koma potibe pachimalawi kukambirana ndikotheka koma phone yi ilibe vuto linalilironse,ndalama yangokhala kuti ikufunika fast, interested customer aimbe kapena WhatsApp # iyi 0988179492,Zikomo

17/08/2026

"Chi Ibrahim Swed chi kwatsalaku tichita ukakamiza kuti ifeso akabaza chim'bale tcheya wathu" Tikudutsa pa Mpenya bridge chanjinga china chimauza nzake Ife tangonva nawo😂

16/08/2026

Tonse mma church mo lero pemphero likhare limodzi lopemphelera scorchers basi
Happy Sunday!

Registration ndiye ili Mkati,Kwangotsara 10 slots kuti atseke,kwaonse omwe Ali interested m***a kuimba or WhatsApp numbe...
10/08/2026

Registration ndiye ili Mkati,Kwangotsara 10 slots kuti atseke,kwaonse omwe Ali interested m***a kuimba or WhatsApp number iyi 0981316486 muyankhulanda ndi bambo Calvin Banda omwe akulongosora zama registration

08/08/2026

Address

Nkhotakota

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nkhotakota Entertainment posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Nkhotakota Entertainment:

Shortcuts

Share