31/08/2026
Kodi team ikaluza ndye kuti chotsatila chake ndikupanga suspend coach?
Mighty Wanderers yapanga suspend Bob Mpinganjira amene anali Head coach wa teamyi.
Izitu zachitika angereziwa atachapidwa dzulo ndi ana awo omwe a Ekhaya FC mu ndime yosiriza ya Chikho cha Airtel Top 8..