Nkhani zokoma by ceekay kadawasieh

Nkhani zokoma by ceekay kadawasieh Wasankha page yathu

*๐Ÿ˜ญMISOZI YAMAYI๐Ÿ˜ญ 3*โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธNKHANI IYI WAPEKA NDIKULEMBA NDI CEEKAY KADAWASIEH.*NKHANI ZATHU ZIKUPEZEKA P...
24/04/2026

*๐Ÿ˜ญMISOZI YAMAYI๐Ÿ˜ญ 3*

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ

NKHANI IYI WAPEKA NDIKULEMBA NDI CEEKAY KADAWASIEH.

*NKHANI ZATHU ZIKUPEZEKA PA GROUP LA*
SUPER STORIES

*ADMIN NUMBER*
+27603773303

๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡
Nkhani yathu mu part 2 tinalekeza pakuti, Chodakwa chinati, ngati wopanda kwawo sanapite msiyeni ndimuwotchere momwemo uyu sandiziwa apa ndinaganiza zolowa mu PART 3

*TIPITILIZE MU PART 3*
Ndinali wokwiya kwambiri apa ndinathyola chotseko mpaka kulowa apa ndinalowa ndimafika kuvhipinda komwe amagona apa nkuti malamu anali atangpvala pitikoti uku akukoka chpfunda kubisa thupi kuyamba mumabere uku amulamu alindimantha kuti mwina awagwirira uku akuti,

Mlamu zowona mwafika mpaka pamenepa kulowa kuchipinda osapereka odi zona๐Ÿ˜ข๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

Mlamu wawo anamwa mowa uja anayakha nati, Anthuni simufuna zantendere chomwe mukuแด‹anilira pano ndichani ? ษดแด…ษชษดแดœ แด€ษดแด›สœแดœ แดกแดสษชแด˜แด€ แด‹แดกแด€แดส™ษชส€ษช แดแดœแด‹แดœแดแด€แด˜สœแดœษดแดขษชแด›sแด€ แด€ษดแด€ แดแด€ษขแด€ษดษชแดขษชแด…แดกแด‡ แดกแดสษชแด˜แด€ แดกแดแด›ษช แดแดœแด‹แดœแด‹สœแด€สŸแด€ แด˜แด€ษดแด แดแด‹แดœแด›แด‡แด›แด‡แดขแด€ แดษชษดแด…แด€ สแดแดแดกแด‡ แด€ษดแด€แดกแด€sษชสษชสŸแด€ ส™แด€แดส™แด แด€แดกแด แด‹แดแด…ษช ษชษดแดœ ษดแด…ษช ษชา“แด‡ แดกแดแดแดกแด‡ แด€แดแด€แดกแด€sแดœษดษขษชสŸแด‡ แดษชษดแด…แด€สแด ษดแด…แด€ษดษช? sษชแดกแดœษดแด…แด€ษดษช แดแด‹แดœแด˜แด€ษดษขแด€ แด€แด˜แด€ แดแด€สษช แดกแดสษชแด˜แด€ ษชษดแดœ ? แด„สœแด€ส™แดกษชษดแด แด€ษดแด€ แด€แดขษชแด‹สœแด€สŸแด€ แดษดสแดœแดส™แด€ สแดแดแดกแด‡สษช แดษชษดแด…แด€ แด€แดขษชสŸษชแดแด€ สแดแดแดกแด‡สแด ษชษดแดœ แด˜แด€แด‹ษชสŸแด€ษดษช แดขษชแด˜ษชแด›แด€ษดษช sษชษดแด…ษชษดแดœ แด€ส™แด€สŸแด‡ แด€แด›สœแดœ

แดแด€สษช แด€แดŠแด€ แด€ษดแด€แด›ษช แด‹แดกแด€ แดสŸแด€แดแดœ แดกแด€แดกแด , sษชษดแด…ษชษดษขแด€sษชสแด‡ แด€ษดแด€ ษชษดแด‡ ษดแด…ษชสŸษช แดแดสแด ษดษขแด€แด›ษช ษดแด…ษชแด„สœแดษดแด„สœษช ษดแด…ษชแดขษชแด˜ษชแด›แด€ ษดแด€แดกแด แด‹แดกแด€แด›สœแดœ

แด„สœแด€ส™แดกษชษดแด แดขษชแด˜ษชแด›แด€ษดษช ษดแด€แดกแด แด˜แดแดแด˜แด€ษดแด ?

แดแด€สษช แด€แดŠแด€ แด€ษดแด€สแด‡sแด‡sแด€ แด‹แดœแดกแด€แดœแดขแด€ แด‹แดœแด›ษช แด˜แด€ษดแด ษดแด…ษชแดœsษชแด‹แดœ แด‹แดแดแด€ แด„สœษชแด…แด€แด‹แดกแด€ แด„สœษชแดŠแด€ แด„สœษชษดแด€แดแด‡ษดสแด‡sแด€ ษดแด‹สœแดกแด€ษดษขแดกแด€ แด˜แด€แดแดกแด€สŸแด€ แดœแด‹แดœ แด„สœษชแด‹แดœแด›ษช , แดแดœษดแด›สœแดœ แด‹แดกแด€แด‹แด‡ sแด€sแดแด„สœแด‡ส€แด€ ษดษขแด€แด‹สœแด€สŸแด‡ แด‹แดœสŸษช แดแด…ษชแดแด€ แดกแด€แดขแด€แดษดแด‡ษดษช แด‹แดกแด€ษดษดแดœ แดแด‹แด€า“ษชแด‹แด€ แด€แด˜แด€ แด„สœษชแด…แด€แด‹แดกแด€ แด„สœษชแดŠแด€ แด„สœษชษดแด€สแด€แดส™แด€ แด‹แดœแด›แดœสŸแดœsแด€ แดขแดแด แด€สŸแด€ แดขแด€แดกแด แด˜แด€ษดแดŠแด€ แดœแด‹แดœ แด€ษดแด€ แด€แดŠแด€ แด€สŸษช แด„สœษชสษชแดษชสŸแด‡ ษดแด€แดกแด แด€แด…แดขแดœแด‹แด€ แดœแด‹แดœ แดส™ษชสแด€ษดษข'แด€แดส™แด‡ ษชแดŠแด€ ษชษดแด€สŸษช แดŠษชแดŠษชส€ษชแดŠษชส€ษช แด‹แดœแดแด€ษดษขแด€ แดขษชา“แดœษดษขแด€ แดขแด€แดแด€สŸแด€สแด€ แด€ แด€ษดแด€ แด˜แด€ษดsแด€ส€แดœ แดœแด‹แดœ แด€แด‹แดœสษชแด‹แด€ แดขษชแด˜แด€ษดษขษชแดขแด แดขแด€แด‹แดœแด‹สœษชแด„สœษชษดษช แดแดœษดแด…แดแดกแด€ แดขแดแด‹แด€สแด€แดส™ษชสŸแด€แด˜แด แดœแด‹แดœ ษดแด‹แดœแด›ษช แดแด€สษช แด€ษดษข'แดษดแด แด€แดส™ษชสแด€ ษดษข'แด€แดส™แด‡ แด€ษดส™แดกแด‡ส€แด€ แดœแด‹แดœ ษดแด‹แดœแด›ษช แด€ษดแด›สœแดœ แด€แด›แด€แดขแดœษดษขแดœสŸษชส€แด€ แด˜แด€แดแด€สŸแดแด˜แด€ แดœsษชแด‹แดœแดกแดœ แดœแด‹แดœ แดแด€สษช แดกแดแดแดกแด‡ แด€ษดแด€sแด€สŸแด€ แด€แด„สœษชแด…แด€แด‹แดกแด€ แด„สœษชแดŠแด€ แด€ษดแด€แด›ษช,

แดŠแดsแด‡ แดŠแดsแด‡ ษดแด…ษชแดแด„สœษชแด›ษชแด…แดกแด‡ แดกแด€ษดแดŠษช แดœแด‹แดœแด„สœษชแด›แด€แดกแด แดส€ ษดแด…ษชษดแด‹สœแด€แดขแด€ แดขแด€ษดแดŠษช แดœแด„สœษชแด›ษชส€แด€ แดแดœษดแด›สœแดœ แดกแด€แด˜สœแด‡ แดœสแด แดกแดsแด€สแด€แด‹สœแดœสŸแด€ ษดแด…ษช แด€ษดแด›สœแดœ ? แด‹แดแด…ษช แดแดแดกแด€ แดœแดขษชษดษขแดแด‹สœแด€

*๐Ÿ˜ญMISOZI YAMAYI๐Ÿ˜ญ 2*โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธNKHANI IYI WAPEKA NDIKULEMBA NDI CEEKAY KADAWASIEH.*NKHANI ZATHU ZIKUPEZEKA P...
21/04/2026

*๐Ÿ˜ญMISOZI YAMAYI๐Ÿ˜ญ 2*

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ

NKHANI IYI WAPEKA NDIKULEMBA NDI CEEKAY KADAWASIEH.

*NKHANI ZATHU ZIKUPEZEKA PA GROUP LA*
SUPER STORIES

*ADMIN NUMBER*
+27603773303

๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡
Nkhani yathu mu part 1 tinalekeza pakuti,mchimwene wamakemu anauza mlam wawo kuti akamachoka uku azapeze atuta sanza zawo osamathawa njala nkhondo ya Russia ili paliponse apa atamva izi anangoti mu part 2

*TIPITILIZE MU PART2*

Mayi ana aja anasowa chonena koma kwawo kunali kugwesa misozi mutsaya mwawo uku akuganizira za ana kuti nanga alowera nawo kuti ? pakuti akwawo nawo ankati akunyada safuna kuwathandiza ndalama zafetezereza akunyada poti amuna awo akugwira ma rand apa anaziguda pachifuwa ndidzanja lamanja uku akuti, ooooh ndizichani zikundisatita ine ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญapa ndinatenga phone kuyimbila phone mchimwene womaliza yemwe tinkamvanako apa naye anayakha ,

Hello achimwali! muli mwanji ndi ana kumeneko

m'chimwene moyo wabwino kaya inu ndi amulam

achemwali mkukhala ngati mkulira bwanji?

mchimwene sindikumvesa kuti ndichani ? pano ndikuuzidwa kuti ndichoke omwe ndimakhalira pamudzi palibe ndiye ndipakile zanga zonse

mchemwali bola akusiyani ndimoyo ngati mwaona mkusoweka mtendere inu bwerani pamudzi sititha tonse kenako phone inaduka

mayi aja anakhala amantha apa nkuti transport alibe yoti abwerere kumudzi kwawo ku Mzimba

Nthawi itakwana 8 chidakwa chinabwera uku chikuyakhula mawu apamwamba nati, lero ndikugona mnyumba anasiya mwana wamayi ngati wopanda kwawo sanapite aziwe kuti ndimuotchera nyumba apa ndigagwira chitseko koma ndinaona chili chokhoma apa sinalimbane nawo koma ndinangoganiza zolowa mu part 3

*BY CEEKAY KADAWASIEH*

*๐Ÿ˜ญMISOZI YAMAYI๐Ÿ˜ญ 1*โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธNKHANI IYI WAPEKA NDIKULEMBA NDI CEEKAY KADAWASIEH.*NKHANI ZATHU ZIKUPEZEKA P...
16/04/2026

*๐Ÿ˜ญMISOZI YAMAYI๐Ÿ˜ญ 1*

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ

NKHANI IYI WAPEKA NDIKULEMBA NDI CEEKAY KADAWASIEH.

*NKHANI ZATHU ZIKUPEZEKA PA GROUP LA*
SUPER STORIES

*ADMIN NUMBER*
+27603773303

๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡
Moyo unayamba kulimba pomwe Bambo anatisiya kujoweni komwe anapita kuti akasake kuti mwina nafe nkusithako moyo apa zinali zovuta kumvesa pomwe mayi ankalandila phone ya bambo iwo powona kuti ndiwo pomwe anali malume omwe anawalandila kujoweniko pomwe ankati ,

Pepani mayi kuno bambo achita ngizi kotero ndili kuchipatala komazambiri tiyakhulanabe ,

Mutu wathu unazungulira kusowa chonena apa nkuti amayi amangolira ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ osadya nsima uku akuyimba phone yomwe anatitumizira abambo kuti timvese koma Malume osayakha kenako tinaona phone osagwiraso

Amayi anakhala tsiku lonse osadya kalikonse kamba koti sanamve zosatira zogwira mtima apa nkuti anangophika nsima nkutisiyila patable apa ndimchemwali wanga tinadya chakudya chija kenako tinabwerera ku school

Tinaweruka mochedwa ku school apa nkuti tinali kuma sports apa nkuti nthawi ikuti 7:30 apa tinabwerera kunyumba koma unali ulendo wosamveseseka pomwe titamva kulira kwa gulu pakhomo pakwathu apa pamtima panaguda uku ndikuziyakhukira ndekha nati , yhoooo basi bambo kulibe apa ndinagwira mchemwali wanga pafzanja kufika kuja zinalidi zachisoni kumva kuti Bambo anthu amwalira ku south Africa atawombedwa ndigalimoto ali panjinga apa mayankho amoyo wathu anasowa kamba koto school fees inkachokera kwa iwo nanga apa tigwira mtengo wanji ?

Malume anathangisa zamaliro mpaka anafika koma zopweteka ndizakuti chomwe tinapindula ndi malaya ndi tea wapamaliro omwe tinamwako koma ndalama osaoneka pomwe phekesera inkamveka kuti bambo anali magulu woti kangachepe kanathandizila ife koma malume anathyolera mnthumba ponena pawo ankati ndalama zagwita ntchito yotumizira malito komaso zakudya zonwe ankagwirisa kumudzi komaso ku south africa konko apa nkuti bulu unating'ambadi thiti kutisiya awumphawi kusowa ..comment. box full

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ  โ„•  ๐•    ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ                             *โ„™๐”ธโ„๐•‹-10*                  _______________________     ...
16/04/2026

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ โ„• ๐• ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*โ„™๐”ธโ„๐•‹-10*
_______________________
*LAST - PART*
...........................
๐•Ž๐”ธ๐•ƒ๐”ผ๐•„๐”น๐”ธ โ„•๐•‚โ„๐”ธโ„•๐•€๐•๐•€ โ„•๐”ป๐•€ โ„‚๐”ผ๐”ผ๐•‚๐”ธ๐• ๐•‚๐”ธ๐”ป๐”ธ๐•Ž๐”ธ๐•Š๐•€๐”ผ
*๐”พโ„๐•†๐•Œโ„™ โ„•๐”ธ๐•„๐”ผ* : ๐•Š๐•Œโ„™๐”ผโ„ ๐•Š๐•‹๐•†โ„๐•€๐”ผ๐•Š
*โ„•๐•Œ๐•„๐”น๐”ผโ„ ๐•๐”ธ ๐”ธ๐”ป๐•„๐•€โ„•*
*[ +27603773303]*
โœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธ
Nkhani yathu mu part 6 tinalekeza pakuti ,Memory Anayamba kusanza achule amoyo apa nkuti mu part 10 munali zithu
โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*TIPITILIZE PART -10*

Anthu ena ankaona izi anachita mantha kusiya kupeohera kenako kudabwa dzanja lili kukamwa apa Memory anasaza zithu zodabwisa kwambiri zomwe anthu ankazifunsa kuti zinkatheka bwqnji kulowa muthupi lamunthu zamoyo ? awa nali mwamafunso ena opanda mayankho uku nkuti Natasha akutukuka nthukuta kwinaku akuti,

*Natasha* : Amen koma ntchito inalipo ndipo zikomo kunwamba kuti mukumva mapephero anthu kotero kumwambako kudyere nyama

anthu kunali kuwomba m'manja uku kuli thungululu azibambo malikhweru uku ng'oma zikuyimbidwa kuli chimwemwe kwinaku Mayi a Memory ali amanyazi komaso wodabwa ndizomwe awona pa mwana wawo apa Natasha anapitiliza kuyakhula ndikhamu la anthu nati ,

*Natasha* : Ndikumutenga Natasha monga kale ndipo azikakhala kunyumba kwanga kotero ndi bambo tikathandizane mpaka achile ndapanga izi kuti aziwe kuti ine ndilibe mphamvu yobwezera koma mwini Yekha chauta ngakhale bible limati konda mzako ngati momwe uzikondera mwini apa ndinamugwira paphewa uku ndikuti ,Memo Osadere nkhawa ndiwe sister wanga uku misozi onse ikusikila mtsaya ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

Natasha anatenga onse aja kusatengera kuti ali ndichani apa kunali kuoephela usana ndi usiku mosongozedwa ndi amuna a Natasha apa Memory anabwerera mwakale kotero mwamuna wake james Chuma chija chinatha ataha mtundu onse mpaka anayamba kuwotcha makala

Memory anakhala zaka ziwir ndi.....

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ  โ„•  ๐•    ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ                             *โ„™๐”ธโ„๐•‹-9*๐•Ž๐”ธ๐•ƒ๐”ผ๐•„๐”น๐”ธ โ„•๐•‚โ„๐”ธโ„•๐•€๐•๐•€ โ„•๐”ป๐•€ โ„‚๐”ผ๐”ผ๐•‚๐”ธ๐• ๐•‚๐”ธ๐”ป๐”ธ๐•Ž๐”ธ๐•Š๐•€๐”ผ*๐”พโ„๐•†๐•Œโ„™ โ„•๐”ธ๐•„...
15/04/2026

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ โ„• ๐• ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*โ„™๐”ธโ„๐•‹-9*
๐•Ž๐”ธ๐•ƒ๐”ผ๐•„๐”น๐”ธ โ„•๐•‚โ„๐”ธโ„•๐•€๐•๐•€ โ„•๐”ป๐•€ โ„‚๐”ผ๐”ผ๐•‚๐”ธ๐• ๐•‚๐”ธ๐”ป๐”ธ๐•Ž๐”ธ๐•Š๐•€๐”ผ
*๐”พโ„๐•†๐•Œโ„™ โ„•๐”ธ๐•„๐”ผ* : ๐•Š๐•Œโ„™๐”ผโ„ ๐•Š๐•‹๐•†โ„๐•€๐”ผ๐•Š
*โ„•๐•Œ๐•„๐”น๐”ผโ„ ๐•๐”ธ ๐”ธ๐”ป๐•„๐•€โ„•*
*[ +27603773303]*
โœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธ
Nkhani yathu mu part 6 tinalekeza pakuti ,Memory ndi amayi ake anali wodabwa kuti lyemwe atawapepherere ndi Natasha yemwe anamulanda mwamuna apa munali zithu mu part 9
โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*TIPITILIZE PART -9*

Natasha ataona izi kenako anati ,

*Natasha* : Aleluya mpingo !!!!

gulu linali mu church muja lonse linayakhila limodzi kuti Amen uku akupenya mwachidwi kwinaku atayimika makutu ngati kalulu kuti amvese apa nkuti Natasha anati,

*Natasha* : Anthu amulungu ndati ndikuuzeni chithu chimodzi ndipo just mark my words akuti, ngati wina akukupanga nkhaza usanamulakwire ziwabkuti mdima ungakule bwanji koma kuja komaso pachichewa pali mawu akuti chowuluka chingauluke bwanji koma palitsiku limodzi chimazatera ndipo mogwirizana ndi mawu onsewewa amazayankhidwa ma mwambwi wakuti ,kwanu ndi kwanu mnthengo mudalaka njoka izi zimatathaunza kuti chomwe wachinyoza tsiku lina umazabwerera ndiye mkanyoza wina munthu mukumupanga nkhaza osalakwa tsiku lina amazakhala thandizo lanu iti ndikunena kamba ka omwe mkuchita ndipo tsiku lina ndinazafotokoza kuti Yudasi anali akudya ndi yesu ndiye anamugulisa ndiye inuso azakupwetekeni ndimbale or mzanu izi ndikunena kamba koti ndakhala zaka 10 ndi ndi ukulu waukulu muchifuwa changa kamba koti mzanga yemwe ndinkamutenga mzanga kundilanda mwamuna wanga koma zinanditengera nthawi kuti ndiyiwale koma chauta mosongozedwa ndamuna anga tinayamba kusala kudya mpaka zonse zinapita kotero zonse ndinazisiyila m'mapephero ndikunena kuti mzanga uja ndi uyu koma ndilibe naye chifukwa ndikunena pano mzangayu ayakhula yekha kuti pano ndimwamuna zili bwanji koma ali mu ukapolo ndichifukwa wafika mnyumba muno koter...

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ  โ„•  ๐•    ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ                             *โ„™๐”ธโ„๐•‹-8*๐•Ž๐”ธ๐•ƒ๐”ผ๐•„๐”น๐”ธ โ„•๐•‚โ„๐”ธโ„•๐•€๐•๐•€ โ„•๐”ป๐•€ โ„‚๐”ผ๐”ผ๐•‚๐”ธ๐• ๐•‚๐”ธ๐”ป๐”ธ๐•Ž๐”ธ๐•Š๐•€๐”ผ*๐”พโ„๐•†๐•Œโ„™ โ„•๐”ธ๐•„...
13/04/2026

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ โ„• ๐• ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*โ„™๐”ธโ„๐•‹-8*
๐•Ž๐”ธ๐•ƒ๐”ผ๐•„๐”น๐”ธ โ„•๐•‚โ„๐”ธโ„•๐•€๐•๐•€ โ„•๐”ป๐•€ โ„‚๐”ผ๐”ผ๐•‚๐”ธ๐• ๐•‚๐”ธ๐”ป๐”ธ๐•Ž๐”ธ๐•Š๐•€๐”ผ
*๐”พโ„๐•†๐•Œโ„™ โ„•๐”ธ๐•„๐”ผ* : ๐•Š๐•Œโ„™๐”ผโ„ ๐•Š๐•‹๐•†โ„๐•€๐”ผ๐•Š
*โ„•๐•Œ๐•„๐”น๐”ผโ„ ๐•๐”ธ ๐”ธ๐”ป๐•„๐•€โ„•*
*[ +27603773303]*
โœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธ
Nkhani yathu mu part 6 tinalekeza pakuti ,Memory anati ine ndikungodikirw tsiku lofera mu part 8
โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*TIPITILIZE PART -8*

Chimwemwe atamva zoyakhuka za Memory anapukusa mutu wopanda nyanga uku akuti ,

*Chimwemwe* : Memo ndikuziwa kuti ukudusa munthawi yopweteka komabe usatengere kuti iwe nfi ine sitikuziwana kapena sindine wachibale wako koma nkutheka kuti vutolo ndikhoza kukuthandiza munjira ina ndiye chonde chonde memo ndiuze

Memory atamva izi khosi lake linapotokera komwe kunali amayi ake uku akugwesa misozi kwinaku akuti ,

*Memory* : Chimwemwe or nditakuuza bwanji koma chopulumutsa moyo wanga sindikuchiona kwanga ndikudikira tsiku basi koma zonsezi ndamayi ndipo ndafa kamba kamayi kukonda chuma ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ anachita kumenyesa nkhwangwa pamwala kuti ndikayerekeza kumukana mkazi wamzangayo ine ndikapeze mayi anga omwe anandibereka komaso ndizikawamvera kona phuno salota ndikanaziwa sikanapita ndipo tikulepherela kumufotokoza kwake kuti mwamunayo anali ndani ? pakati pasatanic kapena wokwima popeza nditalowa zipinda ziwiri zosaloledwa kulowa munthu zinali zothu zodabwisa komaso mpamvu zinandithera nditaona makoswe ali kuchipinda kwina atanyamula certificati ya Death kuzandisiyila pakhomo pomwe panali ine apa nkuti ndinapukusa mutu opanda nyanga komabe nditapitilira kuchipinda china ndinali wodabwa khope za akazi ena ali pakhoma konaso khope yanga ili pabokosi apa ndinali ndimafunso wochukuka opanda mayankho mwamafunso ena anali akuti, kodi atsikana ali pakhomapa alikuti ? konaso ndi ndani ake ? nanga bwanji wabisa kuchipinda kosaliwa anthu ? konaso ine nkhope yanga yapezeka bwanji kuno ? cholinga cha.......

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ  โ„•  ๐•    ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ                             *โ„™๐”ธโ„๐•‹-7*๐•Ž๐”ธ๐•ƒ๐”ผ๐•„๐”น๐”ธ โ„•๐•‚โ„๐”ธโ„•๐•€๐•๐•€ โ„•๐”ป๐•€ โ„‚๐”ผ๐”ผ๐•‚๐”ธ๐• ๐•‚๐”ธ๐”ป๐”ธ๐•Ž๐”ธ๐•Š๐•€๐”ผ*๐”พโ„๐•†๐•Œโ„™ โ„•๐”ธ๐•„...
13/04/2026

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ โ„• ๐• ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*โ„™๐”ธโ„๐•‹-7*
๐•Ž๐”ธ๐•ƒ๐”ผ๐•„๐”น๐”ธ โ„•๐•‚โ„๐”ธโ„•๐•€๐•๐•€ โ„•๐”ป๐•€ โ„‚๐”ผ๐”ผ๐•‚๐”ธ๐• ๐•‚๐”ธ๐”ป๐”ธ๐•Ž๐”ธ๐•Š๐•€๐”ผ
*๐”พโ„๐•†๐•Œโ„™ โ„•๐”ธ๐•„๐”ผ* : ๐•Š๐•Œโ„™๐”ผโ„ ๐•Š๐•‹๐•†โ„๐•€๐”ผ๐•Š
*โ„•๐•Œ๐•„๐”น๐”ผโ„ ๐•๐”ธ ๐”ธ๐”ป๐•„๐•€โ„•*
*[ +27603773303]*
โœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธ
Nkhani yathu mu part 6 tinalekeza pakuti ,Mayi a Memory ndi mwana wawo anabwerera kwasing'anga atafika kuja uku kunali zithu mu part 7

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*TIPITILIZE PART -7*

sing'a ga kunali kuyasa moto kuponda pamoto apa nkuti Memory atamukhazika pamtondo nkhuni inali msinsi wakunanda mkhonsi atanuvalaika mankhwala opatikiza ndidothi lapamtumbila uku atagwilizila mphika m'manja apa sing'anga kunali kuvina ng'oma osati masewera usana ndi usiku keanko tsiku lachitatu anatenga magazi ang'ombe kumuikila muphika anagwilizira uja kuti amwe ndipo atamwa ndikumuchekera phini kenako asing'anga anati ,

*SING'ANGA* : Mayi apa mudikiler kwa mixezi itatu kotero mankhwala awa muzikamuphikila phala m'mawa ulionse komaso enawa azikasamba ndipo abwerera mwakale koma mwachita chanzeru kuthamangira naye kuno mukanaluza uyu

Mayi a Memory anathokoza sing'anga uku akupereka malipiro amzimu K2,000,000 uku sing'anga amvekere

*SING'ANGA* : MAYI PONYANI MUPHIKA WAMIZIMUYO UKU NAYE AKUYIMBILA M'MANJA YAMIZIMU NGATI KUTI KWABWERA AMFUMU PAMALO UKU NDIKUWAUZA KUTI NG'OMBEYI INE MUNDIPASEKO MUTU KOMA YONSEYO MUKHOZA KUTENGA MUKADYE NDIWO KOMA MWINI TAMPANGILA MANKHWALA ASAKADYE KAYE ZAMAGAZI KAYA NDI USIPA , MBEWA MPAKA ZITHU ZITASITHA

Mayi a Memory atanva izi anatenga minyendo iwiri kuwapasa pa cump paja kuti adye inayo ananyamulira kunyumba kudya ndikugulisa kuti apeze ndalama ya rent

Mayi a Memory analimbikila zomwe anauzidwa kwasing'anga uja ndipo sangalephera kona zinali zodabwisa kuti mankhwala atha komaso moyezi itatu yadusa zithu sizikusitha apa anaganiza zowona msana wanjira kuti akaziwe vuto ndipo atafika zinali zovuta kumvesa......

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ  โ„•  ๐•    ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ                             *โ„™๐”ธโ„๐•‹-6*๐•Ž๐”ธ๐•ƒ๐”ผ๐•„๐”น๐”ธ โ„•๐•‚โ„๐”ธโ„•๐•€๐•๐•€ โ„•๐”ป๐•€ โ„‚๐”ผ๐”ผ๐•‚๐”ธ๐• ๐•‚๐”ธ๐”ป๐”ธ๐•Ž๐”ธ๐•Š๐•€๐”ผ*๐”พโ„๐•†๐•Œโ„™ โ„•๐”ธ๐•„...
13/04/2026

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ โ„• ๐• ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*โ„™๐”ธโ„๐•‹-6*
๐•Ž๐”ธ๐•ƒ๐”ผ๐•„๐”น๐”ธ โ„•๐•‚โ„๐”ธโ„•๐•€๐•๐•€ โ„•๐”ป๐•€ โ„‚๐”ผ๐”ผ๐•‚๐”ธ๐• ๐•‚๐”ธ๐”ป๐”ธ๐•Ž๐”ธ๐•Š๐•€๐”ผ
*๐”พโ„๐•†๐•Œโ„™ โ„•๐”ธ๐•„๐”ผ* : ๐•Š๐•Œโ„™๐”ผโ„ ๐•Š๐•‹๐•†โ„๐•€๐”ผ๐•Š
*โ„•๐•Œ๐•„๐”น๐”ผโ„ ๐•๐”ธ ๐”ธ๐”ป๐•„๐•€โ„•*
*[ +27603773303]*
โœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธ
Nkhani yathu mu part 4 tinalekeza pakuti James anali wolusa uku akunjenjemera uku akuyakhula mawu akutu, Memory wandilasa munthiti ndipo palibe yemwe anandipanga chipongwe ngati ichi ndipo dikila ndikuonese mu part 6

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*TIPITILIZE PART -6*

nditagwira kale pistoni (futi) kenako ndinaziyakhula muchifuwa changa natu , mission iyi sinauzidwe paja anati nditizapha munthu ndikawuzidwa apa ndinasiya kukhethyemula futi ija uku misozi ili yhooooo ikugwera mtsaya mwanga kwinaku ndinayamba kuyakhula mwaukali uku ndikutenga zikwama zamalaya ake kuti atuluke azipita kwamakolo ake ndipo samasamala ndimaonekedwe achilendo omwd anali nawo apa Memory amangolira ma card a ku bank analandidwa uku akulira ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

James mwaukali anatenga na key agalimoto yake ulendo uku akuti , ndikamachoka uku ndisakupeze ngati ukuchita makani ziwa kuti nbalame sizilima ndipo ukakhaka chakudya chambalame komasi ntchenche komwe ndikakutaye kunkhalango yawiliranji

Memory misozi sinkakata maso mwake apa nkuti ulemero anali nawo watha kwinaku akuti muchifuwa chake , koma mlungu kundipulumusa apa na ine sindizapangaso mistake yosilira ya anthu wolemerawa omwe aki ndi galimoto apa ndachimina zoona ine kulanda mzanga osatiwa ndikuzilandila mavuto ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ zonsezi ndi amayi kufuna wolemera ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

Ndinakumbukira nawu a james aja akuti ndizakhala chakudya chazinyama kuphatikizira mbalame apa ndizingopita kwathu apa ndinayamba kulongeza sanza zanga kenako ndinayitana wakabaza akanditaye mu bus deport ndalama yomwe ndimati ya saloon komaso yokagayisila kuchigayo ndiyimene ndigwiritse ntchito ngati transport apa ndinaitana wakabaza pagate paja.....

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ  โ„•  ๐•    ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ                             *โ„™๐”ธโ„๐•‹-5*๐•Ž๐”ธ๐•ƒ๐”ผ๐•„๐”น๐”ธ โ„•๐•‚โ„๐”ธโ„•๐•€๐•๐•€ โ„•๐”ป๐•€ โ„‚๐”ผ๐”ผ๐•‚๐”ธ๐• ๐•‚๐”ธ๐”ป๐”ธ๐•Ž๐”ธ๐•Š๐•€๐”ผ*๐”พโ„๐•†๐•Œโ„™ โ„•๐”ธ๐•„...
11/04/2026

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ โ„• ๐• ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*โ„™๐”ธโ„๐•‹-5*
๐•Ž๐”ธ๐•ƒ๐”ผ๐•„๐”น๐”ธ โ„•๐•‚โ„๐”ธโ„•๐•€๐•๐•€ โ„•๐”ป๐•€ โ„‚๐”ผ๐”ผ๐•‚๐”ธ๐• ๐•‚๐”ธ๐”ป๐”ธ๐•Ž๐”ธ๐•Š๐•€๐”ผ
*๐”พโ„๐•†๐•Œโ„™ โ„•๐”ธ๐•„๐”ผ* : ๐•Š๐•Œโ„™๐”ผโ„ ๐•Š๐•‹๐•†โ„๐•€๐”ผ๐•Š
*โ„•๐•Œ๐•„๐”น๐”ผโ„ ๐•๐”ธ ๐”ธ๐”ป๐•„๐•€โ„•*
*[ +27603773303]*
โœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธ
Nkhani yathu mu part 4 tinalekeza pakuti Memory anagwesa nkhope yake ataona zomwe samayembekezera muzipinda muja apa ananyamuka ulendo wolowa mu part 5

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*TIPITILIZE PART -5*


Ndinali wonjenjemera komaso wamantha apa ndinaziguda pamtima ndi dzsnja langa lamanja pachifuwa uku ndikuziyankhulira ndekha ndekha kodi akazi ndaona paja anamwalira ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ koma ndiksnaziwa sikanachita apa ndazikumbira dzenje ndekha apa ndazilandira mavuto uku misozi ikusikila mtsays ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

apa nzeru zinandithera kamwa kumanjenjemera uku misozi sikukata m'maso mwanga๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ apa ndinanyamuka ulendo kuchipinda chomwe ndimagona koma ndinali wamatha komaso wodabwa kuona pazenera yakuchipinda nkhungu ndibtsisi litasitha apa ndinali munthu wowoneka wowoneka ngati munthu yemwe nkhungu yake likupita kwachizungu tsitsi litasithika apa ndinaponya phone pansi kuona maloza omwe ndaona uku ndikumva chitseko chikutsegulika mwamphamvu uku james anali ataziwa apa nkuti anayamba kuyakhula mwaukali nati ,

*James* : Mwana wahule iwe wachita chani ? oooh no no apa or kupha munthu ndikhoza kupha zoona kusokoneza zithu zomwe zimapangisa kuti ndikhale munthu ishiiii

james analunjika kuchipinda apa nkuti Memory anatenga phone yake pomwe anagwesa apa anayamba kulembela massage amayi uku misozi ili m'maso ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

Mayi a memory ataona massage ya mwana wawo anayamba kuwerenga nati,

*_Amayi mwandipha ndipo mwandigulisa kamba kandalama kotero zoti ndikhalaso moyo ndakayika ine mawa ndikufa ndipo bokosi muguliretu_*

Mayi a memory mtima sanaupeze ndipo chomwe ankatathsuza mwana wawo sankaziwa apa anayesera kuyimba kuti aziwe.......

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ  โ„•  ๐•    ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ                             *โ„™๐”ธโ„๐•‹-4*๐•Ž๐”ธ๐•ƒ๐”ผ๐•„๐”น๐”ธ โ„•๐•‚โ„๐”ธโ„•๐•€๐•๐•€ โ„•๐”ป๐•€ โ„‚๐”ผ๐”ผ๐•‚๐”ธ๐• ๐•‚๐”ธ๐”ป๐”ธ๐•Ž๐”ธ๐•Š๐•€๐”ผ*๐”พโ„๐•†๐•Œโ„™ โ„•๐”ธ๐•„...
09/04/2026

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ โ„• ๐• ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*โ„™๐”ธโ„๐•‹-4*
๐•Ž๐”ธ๐•ƒ๐”ผ๐•„๐”น๐”ธ โ„•๐•‚โ„๐”ธโ„•๐•€๐•๐•€ โ„•๐”ป๐•€ โ„‚๐”ผ๐”ผ๐•‚๐”ธ๐• ๐•‚๐”ธ๐”ป๐”ธ๐•Ž๐”ธ๐•Š๐•€๐”ผ
*๐”พโ„๐•†๐•Œโ„™ โ„•๐”ธ๐•„๐”ผ* : ๐•Š๐•Œโ„™๐”ผโ„ ๐•Š๐•‹๐•†โ„๐•€๐”ผ๐•Š
*โ„•๐•Œ๐•„๐”น๐”ผโ„ ๐•๐”ธ ๐”ธ๐”ป๐•„๐•€โ„•*
*[ +27603773303]*
โœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธ
Nkhani yathu mu part 2 tinalekeza pakuti Memory anagwesa nkhope yake pansi uku akuzikanda zala zakumwendo kwinaku akuyakha mayi ake mu part 4 kuti......

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*TIPITILIZE PART -4*

*Memory* nda nda ndamva uku misozi ikusika m'maso ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

mnyumba munali chisangalaro uku amayi a Memory akujowera uku kwinaku James akujowera uku kuzamu huga Memory uku akuyakhula motama kuti tsopano wawina chigayo uyu ndi nyale ndipo sagulaso nyale yowunikila mnyumba azikawunikila yemweyi apa panli chakudya chamadzuro uku nkuti mzake zakudya chakudya Natasha kulakalaka kufa kuti ayiwale zonsezi

Masiku nathera kuchitseko paja amati kwafa ng'ombe sikusowa apa phekesera inamufikira Natasha kuti mzako ponda apa nane mpondepo wakulanda mwamuna apa Natasha anazigunda pamtima ndifzanja lake uku akuti , ooooh God ndimalakwisa chani ? kuti Memory yemwe ndimamutenga mng'ono wanga kapena mkuru wanga kunditere ?๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ ndisanje zanji izi ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ Mlungu wanga mwalolelanji kuti ndisuzike chonchi nthawi yonseyi ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ apa ndinawayitana mayi kenako ndinawauza kuti ,

*Natasha* Amayi chimwemwe chomwe ndinali nacho ndalandidwa ndimzanga yemwe ndimaona nfati ndimbale ndiye kuti ndikhale ndimoyo sindikufuna kuti ndione nyasi timenezi tisamukire kutali ndideali chonde anayi ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

mayi a Natasha anali ndimantha uku anayamba kupepha transfer poti anali aphunzitsi mpaka zinatheka apa nkuti chintake chinasokonekera mpaka kuchotserana ma nunber mu phone

Memory ndi james kunali kunjoya osati masewera kenako James sanachedwe mpaka ukwati woyera apa kunazaza osati masewera

Banja anayamba kukhala patangodusa zaka ziwiri apa nkuti Memory minba akatenga......

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ  โ„•  ๐•    ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ                             *โ„™๐”ธโ„๐•‹-3*๐•Ž๐”ธ๐•ƒ๐”ผ๐•„๐”น๐”ธ โ„•๐•‚โ„๐”ธโ„•๐•€๐•๐•€ โ„•๐”ป๐•€ โ„‚๐”ผ๐”ผ๐•‚๐”ธ๐• ๐•‚๐”ธ๐”ป๐”ธ๐•Ž๐”ธ๐•Š๐•€๐”ผ*๐”พโ„๐•†๐•Œโ„™ โ„•๐”ธ๐•„...
09/04/2026

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ โ„• ๐• ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*โ„™๐”ธโ„๐•‹-3*
๐•Ž๐”ธ๐•ƒ๐”ผ๐•„๐”น๐”ธ โ„•๐•‚โ„๐”ธโ„•๐•€๐•๐•€ โ„•๐”ป๐•€ โ„‚๐”ผ๐”ผ๐•‚๐”ธ๐• ๐•‚๐”ธ๐”ป๐”ธ๐•Ž๐”ธ๐•Š๐•€๐”ผ
*๐”พโ„๐•†๐•Œโ„™ โ„•๐”ธ๐•„๐”ผ* : ๐•Š๐•Œโ„™๐”ผโ„ ๐•Š๐•‹๐•†โ„๐•€๐”ผ๐•Š
*โ„•๐•Œ๐•„๐”น๐”ผโ„ ๐•๐”ธ ๐”ธ๐”ป๐•„๐•€โ„•*
*[ +27603773303]*
โœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธ
Nkhani yathu mu part 1 tinalekeza pakuti mayi a Memory atauzidwa zoti achite pokatenga panti apa sanachedwe koma kuyamba ulendo wolowera mu part 2

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*TIPITILIZE PART -3*

Memory anagwira mutu ngati kuti ufuna kugwa apa maganizo anazaza m'mutu kwinaku akuzipasa mafunso opanda mayankho ,kodi izi ndikuwonazi ndili kumaloto kapena ndizoona ? kodi amayi ali serious ndi izi ? ooooh mlungu wanga zowona tidane ndi Natasha kamba ka mwamuna ? amayi aganiza bwanji ? uku ndikuona akundigwedeza mutu uku akuti,

*Mayi a Memory* Memory osangoti chete apa ngati ukuganizapo zanzeru eni tenga izi ndipo ukuyenera upange izi , utenge panti uyu ndikuthira madzi uzitikita mochapa uku ukunenelera ngati momwe ndakufotokozera muja changu paja azako sakhala kwawo anakhala ngati anadya matako agalu azibwera pompano

Memory anapanga kamba kokakamizidwa komaso kufuna kusangalasa mayi ake uku akuti mumtima bola zisatheke apa anayika panti kuchipinda chamayi ake kuti Natasha asawuwone poti kuchipinda kwamayi safikako Natasha koma changa popezs timalowerana

panti unayanikidwa kuchipinda masiku nathera kuchitseko apa zithu zinayamba kusitha komaso kutembenuka ndipo James mwamuna wa Natasha anayamba kumpezera zifukwa Natasha pomuwona kuipa kuti ndi duntu(wonenepa) komaso ndiwosawoneka bwino apa Natasha anali wodabwa kuyamba kuzifunsa mafunso opanda mayakho ,kodi James zonsezi waziziwa liti? komaso wamunamiza izi ndani ? apa ndinangoti , kwagwa mtengo wanthambi sikusowa utsi suchoka kopanda moto tiziwona mlungu ndimzimbe amakomera aliyense uku misozi ikuchucha maso mwake ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

Memory anali wamantha komaso wamanyazi mzake atamudadaulira......

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ  โ„•  ๐•    ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ                             *โ„™๐”ธโ„๐•‹-2*๐•Ž๐”ธ๐•ƒ๐”ผ๐•„๐”น๐”ธ โ„•๐•‚โ„๐”ธโ„•๐•€๐•๐•€ โ„•๐”ป๐•€ โ„‚๐”ผ๐”ผ๐•‚๐”ธ๐• ๐•‚๐”ธ๐”ป๐”ธ๐•Ž๐”ธ๐•Š๐•€๐”ผ*๐”พโ„๐•†๐•Œโ„™ โ„•๐”ธ๐•„...
09/04/2026

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ[ *๐•Š ๐”ธ โ„• ๐• ๐”ผ* ]โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*โ„™๐”ธโ„๐•‹-2*
๐•Ž๐”ธ๐•ƒ๐”ผ๐•„๐”น๐”ธ โ„•๐•‚โ„๐”ธโ„•๐•€๐•๐•€ โ„•๐”ป๐•€ โ„‚๐”ผ๐”ผ๐•‚๐”ธ๐• ๐•‚๐”ธ๐”ป๐”ธ๐•Ž๐”ธ๐•Š๐•€๐”ผ
*๐”พโ„๐•†๐•Œโ„™ โ„•๐”ธ๐•„๐”ผ* : ๐•Š๐•Œโ„™๐”ผโ„ ๐•Š๐•‹๐•†โ„๐•€๐”ผ๐•Š
*โ„•๐•Œ๐•„๐”น๐”ผโ„ ๐•๐”ธ ๐”ธ๐”ป๐•„๐•€โ„•*
*[ +27603773303]*
โœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธโœ๏ธ
Nkhani yathu mu part 1 tinalekeza pakuti mayi a Memory atauzidwa zoti achite pokatenga panti apa sanachedwe koma kuyamba ulendo wolowera mu part 2

โ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธโ™ฆ๏ธ
*TIPITILIZE PART -2*

Mayi a Memory asanafikile kunyumba apa anapanga chiganizo chopita kunyumba kwa Natasha ndipo atafika anayamba alowa muchipinda cha Natasha uku akuitana nati , Tasha๐Ÿ—ฃ๏ธTasha๐Ÿ—ฃ๏ธ

Mayi a Natasha anali aliku kutchini uku nawo akuyakha komaso kutengera kuti aaaa alowa monga mwamasiku onse osaziwa kuti maganizo amzako nditsidya lina lamadzi apa nkuti nawo akuti , asisi amenewotu atengana ndinjonda yawo akuti akupita ku town akukagula za birthday ya Natasha

Mayi a Memory atamva mayakhidwe amayi a Natasha sanachedwe kuchipinda kuja uku akuchotsa chovala chamkati cha Natasha kubisa muphinifolo ulendo wakukitchini uku akuyakha natu,

*Mayi a Memory* : asis kuteloko ndimayang'ana iyeyu kuti ndimuuze za Birthday yamzake poti awuzana kale ayi basi nanga mwaphika chani ?

*Mayi a Natasha* : a sisi ndaphika mnkhwani ndi nsomba izo dikilani ndiyitereke mudyeretu ngati kuti muli ndi mwana wamng'ono paja a Tasha ikawapola njala akaziphikila wokha

phwete linali pakamwa pa awiriwo uku mayi a Memory mumtima akuti , usandichedwese nthawi sili mbali yanga apa ndikufuna kubwerwra kwasing'anga apa nkuti akuyakha azawo nati, asisi kwa lero sindidikila pomwe mwati akupita kwathu ndiye alendowo akandipeze inu ticheza apa ndinawuyamba wakwasing'anga ndipo nditafika asing'anga anandouza kuti nditenge mankhwala omwe ndikathile muphika omwe unaphikidwapo kwambiri ndipo unada kwambiri kenako ndikatenge madzi apansinje omwe amayenda ndikukathilamo mankhwalawo........

Address

Credi Gauting
Johannesburg

Telephone

+27634466044

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nkhani zokoma by ceekay kadawasieh posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

//iconSize: [32, 32], //html: '' }) .bindTooltip(name, { //permanent: true, direction: 'bottom', //offset: L.point(12, 25), //opacity: 0.88, interactive: true }) .bindPopup(name); markersLayer.addLayer(marker); } function getMore() { if (gettingMore) { return; } gettingMore = true; var center = map.getCenter(); $.ajax({ url: "/vicinitysearch", data: { lat: center.lat, lng: center.lng, country: "SOUTH AFRICA" } }) .done(function(data) { var added = 0; data.forEach(function(loc) { if (!locationIds.includes(loc.id)) { var mapLoc = {id:loc.id,lat:loc.latitude,lng:loc.longitude,title:trunc20(loc.name),popupHtml:loc.popupHtml,urlPath:loc.urlPath,pictureUrl:loc.pictureUrl}; locations.push(mapLoc); locationIds.push(loc.id); map._addMarker(mapLoc); added++; } }); }) .always(function() { gettingMore = false; }); } map._clearMarkers = function() { markersLayer.clearLayers(); } }); }, 4000); });