DAVID ERIC POET

DAVID ERIC POET ● Author
● Artist
● Advocate
(1)

17/06/2026

Kuipa 5 kokhala single, kapena kukhala wopanda wa chikondi kungasokoneza bwanj moyo wanu ? Five things 👇

16/06/2026

Kodi ndi zoona kuti nkazi akhoza kumukana mwamuna chifukwa cha mfundo zake zosagwira mtima?

[From inbox 📥]"Hello Eric, Nkazi yu ndimamukonda, khalidwe lake labwino, maonekedwenso a nyatwa, mbina , ma hip ali nazo...
15/06/2026

[From inbox 📥]
"Hello Eric,

Nkazi yu ndimamukonda, khalidwe lake labwino, maonekedwenso a nyatwa, mbina , ma hip ali nazo..

Ndilibe naye vuto kwambiri, ndayesesa kumuphunzisa kaphikidwe kabwino, komabe zikuvuta kwambiri, sakukwanitsabe. Ndinamutumiza ku mudzi mlamu wanga winawake amaphika bwino kuti akaphunzire komabe mmm sizikuyenda amwene.

Dzulo Sunday, ndnamuza aphike nsomba za fresh ,ndnazisowa. Vuto ndinachokapo kae. Amwene ine kufika kupeza nsomba izi , ndnajambula kuti ndikalemba nkhani yi anthu aone zomwe nkaziyu amaphika.

Panopa ndikuganiza zomusiya, even a kwathu avomerezaso kt sizoona, koma ma video ako Eric amandiphuzisa chikondi cheni cheni , ndye apa ndili wobalalika."

Apange bwanj zathuyi?

14/06/2026

Good afternoon, Chonde akazi si amuna onse amene amafunsira nkazi kufuna kungomuyesa.
Amuna ena amakhala akufunsira ambiri pakamodzi. Ndye musamakane mopitilira, kudikira kuti mulolabe, muzafana nayo.

14/06/2026

Ubwino wokhala mu Relationship, zinthu 6 izi 👇 osangoona zofooka. Mu chikondi muli ubwino wochuluka.

14/06/2026

Akamati amuna kapena akazi onse ndi chimodzimodzi , inuyo mumagwirizana nazo?😔 ine ndi ayi

13/06/2026

Mungamchite chani mwamuna wanu atasilira nkazi wina inu muli pompo?😔

13/06/2026

Good Morning, Kodi pali vuto nkazi kumuchapa makofi mwamuna akalakwisa?😟

12/06/2026

Good morning, Kodi nzotheka nkazi kukana mwamuna woti kwao kuli fridge?😔

Address

15 Railway Street
Johannesburg Central
2092

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DAVID ERIC POET posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to DAVID ERIC POET:

Share