13/12/2025
NKHAN YOMVESA CHISONI YOMWE YACHITIKA KU CAPE TOWN
Nkhani ik*t anthuwa anakumana ku cape town mamunayo ndiwaku kasungu mkaziyo waku Blantyre onse amakhala ngat mwabanja mpaka anabalilana mwana kenako amunawo anagula malo koma akaziwo amakakamila k*t malo asainidwe mudzina lawo chifkwa chot abambo akana basitu mkangano ali mkati mokangana amayiwo anangotenga madz amoto ndkuwathila abambowo mmene mukuonelamo zosaendatu.
chenjelani ndmabanja ongokumana ku South Africa kuno mufapo zaziiii