Azonto Malawi

Azonto Malawi kuseka mpaka mmimba kupweteka

Palibeso za DNA apa mwana ndiwanga uyu eti Angoni moti ndunama achemwa?🤣🤣
30/08/2026

Palibeso za DNA apa mwana ndiwanga uyu eti Angoni moti ndunama achemwa?🤣🤣

30/08/2026

Join my WhatsApp group ngat mukufuna video yamzimayi emwe wagwidwa ndchigololo ku Cape town coz anthu mukundivutisa kwambri link ndiyomweyo

kungoona dress lokhalo mwakumbukila film yanj?
30/08/2026

kungoona dress lokhalo mwakumbukila film yanj?

Basitu Chathapo!!! Vuto Ndi Onesmus 🤣🤣🤣
30/08/2026

Basitu Chathapo!!! Vuto Ndi Onesmus 🤣🤣🤣

Mutati kumpanda kwa bwana wanu mwapezako  ndalama chonchi iwowo akugona mungapange bwanj kukawauza kapeza kusanduka sata...
30/08/2026

Mutati kumpanda kwa bwana wanu mwapezako ndalama chonchi iwowo akugona mungapange bwanj kukawauza kapeza kusanduka satana bas?🤣🤣🤣

Koma azimayi chimakhala chili chani kapena kufuna kuiphula mwachangu? nde ndi izi mpaka akunyenganitsani pagulu anthu ak...
29/08/2026

Koma azimayi chimakhala chili chani kapena kufuna kuiphula mwachangu? nde ndi izi mpaka akunyenganitsani pagulu anthu akuona

Tiyeni tikambilane apa,, Kod chilango chomwe mwamuna wamzimayiyu ndchabwno kapena samaenela kulangidwa choncho?

Short Story 🤣🤣🤣
29/08/2026

Short Story 🤣🤣🤣

lingakhale boma lanji ili ku Malawi ko?
29/08/2026

lingakhale boma lanji ili ku Malawi ko?

kuchenjela kwa munthu olemela wina mmalo molemba ntchito azilonda k*t azilondela nyumba yake mmalo mwake iyeyo anangogul...
29/08/2026

kuchenjela kwa munthu olemela wina mmalo molemba ntchito azilonda k*t azilondela nyumba yake mmalo mwake iyeyo anangogula Wi-Fi ndkuiyika yaulele moti anthu akuchezela panja pa nyumba yake chfkwa chongofuna Wi-Fi yauleleyo mwni nyumba pheeeee mnyumba kuswa tulo azilonda aulele ali panja usiku onse chfkwa cha Wi-Fi 🤣🤣🤣🤣 chithuzi ichi chinatoledwa around 4:45Am m'banda kuchatu umenewo 🤣🤣

Kod ndi Nsomba yanji iyi odziwanu?
29/08/2026

Kod ndi Nsomba yanji iyi odziwanu?

Address

VICTORIA Street
Durban

Telephone

+27699510650

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Azonto Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Azonto Malawi:

Shortcuts

Share

Category