Nazrul Siraaj

Nazrul Siraaj Malawian based Nasheed Artist.

Mnyamata tsopano akudxanso ndiina Yasin Jiah 👑🔥
30/05/2026

Mnyamata tsopano akudxanso ndiina Yasin Jiah 👑🔥

10/05/2026

Ati ndine Black mambazo 😂😂😂😂

Kuti Deen yi tiimvetsetse Choyamba Tidziwe kuti Chisilamu ndichaniIzi ndi kunena kamba kakuti asilamu ambili sitimadziwa...
20/04/2026

Kuti Deen yi tiimvetsetse Choyamba Tidziwe kuti Chisilamu ndichani
Izi ndi kunena kamba kakuti asilamu ambili sitimadziwa kuti kodi chisilamu kapena kuti kukhala msilamu ndichan

Ambili timazitcha asilamu kumachita kuti sitichita zomwe Allah anatilamula kuti tizichita.

Chachiwili tikuyenela kudziwa chifukwa chomwe Allah anatilengela then titha kumalowa ku zinthu zina Koma izizi titazivetsetsa kaye.

Chachikulu tiyeni Tiimphunzile bwino Deen yi komaso Tiwaphunxitse Ana athu komaso okondedwa athu

18/04/2026

Tsiku lina ndizaponya zija mumapanga ku studio zija Apo biii mundichune Kena kake
😂😂😂

*MALAWI ISLAMIC ARTS*Malawi Islamic Arts ndi tsamba lomwe limathandiza Achinyamata aluso kuti afikile anthu ochuluka muk...
15/04/2026

*MALAWI ISLAMIC ARTS*

Malawi Islamic Arts ndi tsamba lomwe limathandiza Achinyamata aluso kuti afikile anthu ochuluka mukamphindi kochepa ndipo ndi tsamba lokhalo la pa internet lomwe lili ngati nkhokwe yopezela mitsangalutso yosiyana siyana komanso Zina zokhudza Chikhululupiliro Cha Chisilamu.

Monga mukudziwa tsambali limapezeka ndi zinthu Monga:

- Ma Ulaliki (Bayan)
- Quran (yotanthauzila muchichewa komaso Chizungu
- Ndakatulo
- Ma Nasheed

ndizina zambili.

Pakufuna kupitiliza ndi zintchito zimenezi komaso Kuthandiza Achinyamata aluso muno MMalawi, tsopano pa tsambali Achinyamata Aluso atha Kutsekula account yomwe iziwapatsa mwayi opanga:

1. Kuika zinthu pa Internet (Mwaokha
2. Kugulitsa komaso kukhazikitsa mitengo ya Ma luso awo
3. Kuona momwe Maluso awo akuchitila patsambali monga kuona chiwelengelo Cha ovela, Ogula komaso omwe apanga download Maluso awo.
4. Kutha kulumikizitsa zinthu zawo ndi tsamba la *YouTube* kuti zisavute kagawidwe.

Zakhale nafe Limodzi pa Mkumano wapa Internet omwe tizakhale tikuonetsa kaonekedwe Ka tsopano Ka website komanso Kuphunzitsa kapangidwe upload kazinthu zanu.

Tsikundi pa *25 April* kudzera pa *Google Meet.*

Kuti mudziwe zambili tipeze pa
WhatsApp: +265 998 737 873

Malawi Islamic Arts
Provision of dhikr through Arts

14/04/2026

Of cause Amati tiziyankhulana mu zolakwa komaso kumakumbutsana ndizabwino kwambili Koma Tima Sheikh Content creators Tachuluka pa social media pano nditongofuna attention Chabe.

Don't get me wrong Ma sheikh Ena pano akamayankhula amayankhula zinthu motsatila Qur'an ndi Sunnah Pomwe Ma content creators akungobwebwetuka posadziwa chomwe akunena.

Nde kwaiwe bale wanga amene umangoti poti uyo Amavala mkanjo ndi shehe ndimutsate aaaaa iwe utsata zosatsata zili zabwino kwambili kwaiweyo kuti uiphunzile Deen yi kuti uzindikile than kungopanga follow zinthu zomwe ulibe Nazo kuzindikila

Lero ndipa 7th April tsiku lomwe ndinabadwa Alhamdulillah.Koma nditengelepo mwayi pa tsikuli pokuyamikani nose ndinso ku...
07/04/2026

Lero ndipa 7th April tsiku lomwe ndinabadwa Alhamdulillah.

Koma nditengelepo mwayi pa tsikuli pokuyamikani nose ndinso kukupemphelani zabwino kwa Allah kuti azikudalitsani ndinso kutikhululukila mu zolakwa zathu

Komanso timupemphe Allah kuti awafewetsele asilamu Onse omwe kukumana ndi zonkhoma padziko pano komaso kuwachitila chifundo abale athu aku Iran, Palestine, Sudan ndi Maiko Ena omwe akuvutika ndi nkhondo.

اللهم امين

Za Lailack Color 😂 tikambabe nkhani ilipo apa ndiyoti Kuli mpunga wa nyama kwa Muhammad Alli TikadyeIne monga shawish wa...
01/04/2026

Za Lailack Color 😂 tikambabe nkhani ilipo apa ndiyoti Kuli mpunga wa nyama kwa Muhammad Alli Tikadye

Ine monga shawish wamkulu nduti nose mubwele

Congratulations bro

Big shout out to my newest top fans! 💎 A***n Ashraf, Vasco Jassias, Hussain Banda, Japhali Ayoub Tim, Isher Siraj, Alick...
01/04/2026

Big shout out to my newest top fans! 💎 A***n Ashraf, Vasco Jassias, Hussain Banda, Japhali Ayoub Tim, Isher Siraj, Alick JamesOmar Ibn Hassan, Khadijah Lapken, Mwawi Mfune, Enock Nick Chitemwe, Aesha Thameen Alvin Balala, Moms Hashir

Drop a comment to welcome them to our community,

Address

153A Taronga Road
Cape Town
7764

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nazrul Siraaj posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Nazrul Siraaj:

Share