Chindiwo BROTHERs

Chindiwo BROTHERs for entertain

01/09/2023

Wawa people
Lets chat here🙌🙌

01/09/2023

Ine ndimafusa Map a ku Area 23 kwa Tsikana winawake
Ettin mpaka kukuwa k*t
"Ndati ndili ndi chibwezi kale inee"
😂😂😂😂😂

21/10/2021

made in where?🙆‍♂️🤷🏾‍♂😁🤣🤣

19/09/2021

Mulungu ndi wachikondi komaso sakhumudwisa muloleni k*ti ayendesr tsogolo lanu maphunziro anu ndipo simuzakhumudya konse
Trust Jesus

21/10/2017

(Mateyu 14vs 30_31)apandipamene Petulo anamira panyanja izi zinachitika coz chakuchepa chikhulupiliro ndikukaika.izi zik*tiphuzisa kt tisakhale okaika kaika.Aleluya

11/10/2017

(aEfeso4vs 26)amat kwiyan koma musachimwe zuwa lisalowe muli izi zik*tiphuzisa kt tisamangokwiya kma tizisangalala.Aleluya

01/10/2017

zochitika mwachidule anthu 55 aku Europe agwilizana zot akumbe Nyanja, izi zachitika chifukwa chavuto losowa madzi zikolo. munali ndine muulusi wanu F.C.J

30/09/2017

Tsiku lina F.Chindiwo aphuzisi anamufusa k*t anene chizungu cha aneneri onyenga, iye avekele Sexual in*******se prophet.

Endereço

Ndagoma
Tsangano

Notificações

Seja o primeiro a receber as novidades e deixe-nos enviar-lhe um email quando Chindiwo BROTHERs publica notícias e promoções. O seu endereço de email não será utilizado para qualquer outro propósito, e pode cancelar a subscrição a qualquer momento.

Compartilhar