Khuku za ntown

Khuku za ntown Liti Staff

Ndani amamudziwa uyu?
17/06/2026

Ndani amamudziwa uyu?

Thambo lakuda lagwa pa DomueVasco Luis nnela, opanga malonda pa Domue yemwe amadziwika ndi dzina lakuti Nnela wapezeka o...
09/11/2025

Thambo lakuda lagwa pa Domue

Vasco Luis nnela, opanga malonda pa Domue yemwe amadziwika ndi dzina lakuti Nnela wapezeka opanda moyo tsopano atasowa kwa sabata zitatu. a Nnela amachokela ku buwa m'dela la Domue lomwelo. iwowa anasowa ku Dedza komwe amakhala. iwowa adasamukilako ku Dedzako m'thawi ya ma DEMO kutsatila kuotcheledwa nyumba komaso katundu.

08/11/2025

hi amigos

08/10/2023

Atoht manje oyimba watisiya, kodi ku Malawiko mukuti zikukhala bwanji?

28/06/2023

Tchimo lingavute kothawila nkwa yehov"

29/04/2023

Padja amalawi sitikhalila kuyiwala tikuti AWILO LONGOMBA abweze ndalama dola ikuvuta kumpanje sizodyelanazo

20/11/2022

Nzungu akati
SOME POWER'S

munthu wakuda anvekele
SAMPWAZA

Maluzi akumenya zinthu sizili pabwino, okongola komaso okongoza onde ali mmaluzi. NDE KWA IWE ULINDINGONGOWE? Akupha bas...
18/06/2022

Maluzi akumenya zinthu sizili pabwino, okongola komaso okongoza onde ali mmaluzi. NDE KWA IWE ULINDINGONGOWE? Akupha basi!!!!
kunvela sound latest release ya Sabe-jay - zindipha.

12/03/2022

MrFb Bla akukonzeka kulowa mu studio, anyamaya mukumapita ndi dzakudya ku Studio yeti?? 🤓🤓🤓 ndimpake mukumabwela ndizakuswa

Endereço

Tete

Website

Notificações

Seja o primeiro a receber as novidades e deixe-nos enviar-lhe um email quando Khuku za ntown publica notícias e promoções. O seu endereço de email não será utilizado para qualquer outro propósito, e pode cancelar a subscrição a qualquer momento.

Compartilhar

Categoria