Child Love Story by Sdjč NgōPhī

Child Love Story by Sdjč NgōPhī Kusangalatsa komaso kuphuzitsa

Lero muli zii pampando kaphepo kayazi yazi kakumenya uko mukudwa cool drink.... Kodi mukudziwa kuti mwapezeka lero chifu...
28/09/2021

Lero muli zii pampando kaphepo kayazi yazi kakumenya uko mukudwa cool drink.... Kodi mukudziwa kuti mwapezeka lero chifukwa chá mlengi wanthu????
Bwanji osangothokoza kuti ambuye zikomo pondifikitsa tsiku larelo,,, alipo ena omwe akuzuzika ndi matenda osiyana siyana,,, ena atsikila kuli chete,,, mpamene iwe ndi ine tikusangalala tizivele chisoni,,, pakuti sife opambana.....

17/05/2021

Yesu wanga ndimbambande amanditetezera usana ndi usiku iye ndi nyali yowunikila tsogolo langa

10/04/2021

∆∆∆ Serch and like child love story∆∆

Partilhe..

Mai: wadzuka bwanji mwana wanga okondedwa??
Mwana: Ndadzuka bwino koma mmmh maganizo andichulukila

Mai: bwanji?? Isakhaletu mimba imeneyo paja ndi boyfriend wako ngophi mumabwela kuja kutada kuchoka kukwaya..
Mwana: ayi amayi sizomwe muganizazo usiku wathau ndinalita zoipa.
Mai: umalota chiyani kapena nfiti amakutambira???

Mwana: aí amai ndinalota munthu wina ali pampando wachifumu, ndipo analamura anthu ake atatu kuti: ayimbe lipenga kusokhanitsa anthu onse apadziko lapasi ndipo zinatheka koma titakhala pang'ono tangoona patulutsidwa mabuku awiri...ndikuyamba kusakha anthu wena ine ndinatsala, amene anasakhidwa anali anthu okwana 500 koma anthu tonse tinatsala,,,, tili chikhalire chomwecho tangoona chinthu chonga moto chikubwela kulunjika anthu tonse,,,ndipamene ndina...

Mai: mwana wanga usatope wamaliza dziko Lino liri pamoto,,amene anali pampando wachifumuwo ndi yesu,,amene anayimba malipengawo ndi angelo,,mabuku amene anatsagulidwawo Lina ndi wosatha,,,linaro (gahena) dziwa kuti si anthu anse omwe amati ambuye ambuye amene adzakalowe kumwamba aí paku atumiki ndi akhristu ndi ambiri koma osakhidwa ndi ochepa..
Mwana wanga okondedwa lapa usiye unchimo pakuti mulungu adzanena mlandu wa zochita zonse ndi zobisika zonse ndi zosabisika zonse ngakhale zabwino ndi zoipa zonse,,,koma ngati ufuna ukapezeke mubuku lamoyo wosatha ukuyenera kutsata malamuro ake 20:1-21 komaso 19:18-20/ 22-36-40
Ukangokwanilitsa izi udzapeza moyo wosatha Poti ndiko lapasi limadana ndi kuunika linakonda mudi ngati galimoto yopanda nyali koma iwe lero Lino sitha zochita zako ndikuvomereza kuti yesu ndiye mpulumutsi wako,, ndipo sudzakhutitsidwa mwana wanga wandiva?

mwana: inde amai ndavetsetsa ndipo kuyambiri lero patsiku ndidzipephera m,mawa masana ndi madzuro pogona ndi kumasala kudya kuti ambuye andikhrulukile pa zakwayipa zanga..

Amai: chauta alemekezeke

Typ Amém 🙏🙏

Ser cacata, não pega mulheres bonitas....
03/04/2021

Ser cacata, não pega mulheres bonitas....

14/03/2021
13/03/2021

Kodi zomwe zimapangitsa kuti nkazi wapabanja azipanga zibwezi zakuseli kumasiya mwamuna wake ndichiyan????
Nb: ndiuzeni ine sindikafuna kuti nkazi wanga adzindizembera..

11/03/2021

Brather king RichieH alipodi padziko pano????????

Atiyiwalatu, nanga bwanji
Chisangalalo Sweetest Stories

Never give up..!
10/03/2021

Never give up..!

Ukakhala duu, kulingalira zanyengo zowawa zomwe ukukumana nazo, usadzidela nkhawa pakuti zamawa sizidziwika ai, yehova a...
05/03/2021

Ukakhala duu, kulingalira zanyengo zowawa zomwe ukukumana nazo, usadzidela nkhawa pakuti zamawa sizidziwika ai, yehova amakhala akukozera njira yoti upezere mdalitso wako, pakuti chikondi chake ndichamuyaya, iye matikonda nthawi zonse ndipo amakhala nafe munyengo zonse pamavuto ndi pantendere, mangotisiya pang'ono kuti atiwone zofooka zatha osayiwala kuti..Ekisodo 15:3 ...yehova ndiwakhondo...

Top a•j•p©sj✓np✓©Sonha e serás livre de espírito...luta e serás livre da vida....!
04/03/2021

Top a•j•p©sj✓np✓©

Sonha e serás livre de espírito...luta e serás livre da vida....!

Endereço

Angònia-Lifidzi
Tete

Notificações

Seja o primeiro a receber as novidades e deixe-nos enviar-lhe um email quando Child Love Story by Sdjč NgōPhī publica notícias e promoções. O seu endereço de email não será utilizado para qualquer outro propósito, e pode cancelar a subscrição a qualquer momento.

Entre Em Contato Com O Negócio

Envie uma mensagem para Child Love Story by Sdjč NgōPhī:

Compartilhar