NyasaPlug

Call Directions Website

NyasaPlug °Updating the public on Entertainment and General news in Malawi and all over the world 🌍.

18/09/2026

Atangoti aliyense afunde ndebvu za amuna ake, ena mukhoza kudwala zibayo.

Deputy IG Noel Kayira aomberedwa pomwe amapulumutsa Nusrat Osman.Wachiwiri kwa mkulu wa apolisi m'dziko muno Noel Kayira...
17/09/2026

Deputy IG Noel Kayira aomberedwa pomwe amapulumutsa Nusrat Osman.

Wachiwiri kwa mkulu wa apolisi m'dziko muno Noel Kayira waombeledwa lero pomwe amatsogolera police operation yofuna kupulumutsa Osman ku Chadzunda (Blantyre).

Padakali pano, a Kayira akulandira thandizo la chipatala pa chipatala china mu mzinda wa Blantyre ndipo omwe anamuba Osman ali muchitokosi cha polisi.

Mchimwene wake wa Osman, Shobi Jiwa watsimikiza kuti m'bale wake ali bwino ndipo wathokoza a Kayira ndi polisi yonse chifukwa cha ntchito yopambana yomwe agwira.

Izi zadza patatha masiku 6 apolisi atalengeza kuti Osman yemwe ndi mzika yaku Britain ndipo amagwira ntchito ngati auditor ku Audit Consult ku Blantyre wasowa anthu ena osadziwika atamuba pa Mount Pleasant (Blantyre).

Apolisi anati apereka K30million kwa munthu yemwe apereke uthenga ogwirika omwe uthandizire kuti Osman apezeke.

Congratulations! Mr Jokes and madam,  kwabadwa baby Aurelius Thonyiwa. Ati wabadwanso opanda Mano.
17/09/2026

Congratulations! Mr Jokes and madam, kwabadwa baby Aurelius Thonyiwa. Ati wabadwanso opanda Mano.

Veteran Nigerian actor and film executive, Oludotun Baiyewu Jacobs, popularly known as Olu Jacobs, has died at the age o...
16/09/2026

Veteran Nigerian actor and film executive, Oludotun Baiyewu Jacobs, popularly known as Olu Jacobs, has died at the age of 84.

In 2021, his wife, actress Joke Silva, revealed that he had been diagnosed with dementia with Lewy bodies, a progressive condition affecting the brain and nervous system.

Jacobs began his acting career in the UK in the 1970's, appearing in TV series including The Goodies, Till Death Do Us Apart, Angels and The Tommorow People.

He later returned to Nigeria, where he became a leading figure in the country's growing film industry.

Source: BBC and Pulse Nigeria

Picture: Late Jacobs and his wife Joke Silva

Khumbo Bonzoe Soko
15/09/2026

Khumbo Bonzoe Soko

Congratulations! Mr & Mrs Chiweza.
14/09/2026

Congratulations! Mr & Mrs Chiweza.

Ladies, pick your number...
14/09/2026

Ladies, pick your number...

Mwapanga kale download Nzika Wallet App?
13/09/2026

Mwapanga kale download Nzika Wallet App?

Happy birthday Miracle Vic Chinga. Your favorite song yomwe anaimba ndi iti ?
13/09/2026

Happy birthday Miracle Vic Chinga.
Your favorite song yomwe anaimba ndi iti ?

13/09/2026

Address

Zomba

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when NyasaPlug posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share