Teamjodan Music Pro

Teamjodan Music Pro For Music Promo,Graphic Design Or Advertising Opportunity On Our Page #0884820164/0983538062
Verifi󱢏 Art
(4)

Inayo ndi profile picture ya Gwamba inayo ndi cover ya ep ya Krazie G. Kwinako muwona nokha kuti chikuchitika ndi chani....
06/05/2024

Inayo ndi profile picture ya Gwamba inayo ndi cover ya ep ya Krazie G. Kwinako muwona nokha kuti chikuchitika ndi chani... 🤣🤣 Ife mabodza ayi

06/05/2024

Olo battery 🪫 lafoni yanu litakhala 2% yokha, 1 minute yokha ndiyokwanira kumthokoza Mulungu chifukwa Cha mphatso yamoyo💝

05/05/2024

📢Mwalandira mphatso yanji
Lero kuchokera
Kwa MULUNGU🥳🙏💕

04/05/2024

Ngati mukuona post yi, Muli Moyo, Healthy, 2min yokha Muyamikeni 😍🙏

03/05/2024

School=AYI
Church= AYI
Mowa= AYI
Zibwezi =AYI
Mpira=AYI
Mumatani kodi?????

03/05/2024

oimba m'modzi yemwe akuoneka kuti apindula kwambili ndi maimbidwe chaka chino😌🔥

03/05/2024

Mulungu Dalisani Dzanja Lililonse Lomwe Lilembe Apa Kuti 😍🙏

02/05/2024

Kodi zimathekanso mkazi kumukana mwamuna oti kwawo kuli Fridge?

 📸 CzarCHenry Czar🔥   ゚viralfbreelsfypシ゚viral
02/05/2024

📸

CzarCHenry Czar🔥

゚viralfbreelsfypシ゚viral

02/05/2024

Eti akulu akulu, 30 days ndiyokwanira kusaka ndalama ya rent?😌

02/05/2024

Ndikuziwa uli pa
Changu🏃‍♂️🏃‍♂️🏃‍♀️🏃‍♀️ Komabe
2 Minutes Yokha Lemba✍
👉“AMEN” 😍🙏,Mulungu Atichitila Zabwino zambili💝💯

Address

Zomba
TEAMJODANENT

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Teamjodan Music Pro posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Teamjodan Music Pro:

Share

Category