14/12/2021
Abale amuna ena ndi panseu akamayenda ndithu ,mkazi kukusiya mpaka kukagona kwa mamuna zako ,kukupezanso iwe kumulandila .koma kwa dimusa mwafasako eti wina kukasekeledwa nyumba kwa ngwelero masana onse akudyedwa ,ashi koma dimusa upole Moto chonde