New Music

Call Directions Contact the establishment

New Music Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from New Music, Mzuzu.

Aluza dala akufuna axakhale ali kwao akapange nawo abahambe pa 30 pano
28/06/2026

Aluza dala akufuna axakhale ali kwao akapange nawo abahambe pa 30 pano

28/06/2026
Pamene boma lapereka ma bus 8 ndipo boma la south Africa lapereka ma bus 10 kutenga anthu omwe aliku south Africa omwe a...
16/06/2026

Pamene boma lapereka ma bus 8 ndipo boma la south Africa lapereka ma bus 10 kutenga anthu omwe aliku south Africa omwe akuchita m'bindikiro pa malo ena otchedwa sherwood mu mzinda wa Durban ku South Africa, Nawo a Shepherd Bushiri akonza ma bus 10 kuti apite akatenge anthu ku South Africa.

Pamene anthu anayamba ma wowowo kuti nchifukwa chani a mipingo sakuoneka kuchita ntchito zachifundo monga a Khristu kunali ziii kufikira tsopano a Bushiri ayankhapo

13/06/2026

Nde lero ofunika tiikwere Morocco kuti xenophobia ipse mtima

12/06/2026

Pamene tikuyandikira 30 June.
Tiphunzirepo kanthu a Malawi nthawi zinaso timaonjedza kutailira kukhala mdziko la eni opanda ma plan ngati kwathu pano zimangokhala ngati kupita kujoni ndi career tsopano. Tiyeni tidzuke inde zinthu zikuvuta kumudzi kuno kma anthu ena anapita ku joni kugwira ndi target zaka 3, 4, 5 kumabwerako kuzayamba kupanga zao pano kuwaona simungakhulupilire zikuwathekera

Apa anthu ena oti analumbira kuti kumudzi azapita 2060 tikunena pano akulembetsa nao kuti akwere nao ma bus aulere azibwelera kumudzi kuzayambiraso pa zero chonsecho mwayi anali nawo opeza capital kma anaseweretsa. Tiphunzirepo apa kwaini ndi kwaini, kwanu ndi kwanu

Ngakhale a za food safety anatsusa kuti mabowu omwe amapedzeka pa tomato amakhala walumidwa ndi njoka kuti ndi zonama, k...
11/06/2026

Ngakhale a za food safety anatsusa kuti mabowu omwe amapedzeka pa tomato amakhala walumidwa ndi njoka kuti ndi zonama, kma anaonjedzera kunena kuti njoka ingathe kuluma tomato pokhapokha ngati yakoledwa ndipo ikulephera ku choka ithadi kuluma kma izi sizimachitikachitika. Komabe anthu azipewa kudya tomato wamtundu oterewu ngakhale chipaso cha mtundu ulionse ngati mwachipedza ndi mabowu otere pewani kudya

Eti inu mukuona bwanji tomato ameneyi amakhala analumidwadi nsi njoka?

07/06/2026

Kwa amene tili kumudzi kufuna kupita ku South Africa pulizi conde dikirani musanyamuke izi zizizile kae. Polani moto kae kulipo kuzangofikira mmanja sikulibwino kujonz

TILI KU MKHOTAKOTA LEROAwa akukakhala ku ndende kwa zaka zitatu akugwira ntchito ya kalavula gaga cifukwa copedzeka olak...
03/06/2026

TILI KU MKHOTAKOTA LERO

Awa akukakhala ku ndende kwa zaka zitatu akugwira ntchito ya kalavula gaga cifukwa copedzeka olakwa ponyenga mbuzi. Mmhuu

Nyama ya nkhumba imakoma ngati nyama ya MunthuIzi zinasimikidzidwa ndi anthu angapo omwe anadyapo nyma ya munthu monga1....
01/06/2026

Nyama ya nkhumba imakoma ngati nyama ya Munthu

Izi zinasimikidzidwa ndi anthu angapo omwe anadyapo nyma ya munthu monga

1. Mtundu wa anthu otchedwa Wari (Wari people) ochokera ku Brazil omwe amadya nyama ya munthu akamwalira ngati njira yoikira maliro. Akhala akupanga zimenezi mpaka zaka za ma 1960s. Tikumbukire kuti pali njira zingapo zomwe anthu pa dziko la pansi amataira munthu akamwalira. Njira yomwe ili common ndiyoikana kumanda koma ena amaotcha thupi la munthu okufa phulusa lake kukataya kunyanja. Mtundu wa Wari umadya thupi la munthu omwalirayo, ndipo anasimikidza kuti nyama ya munthu imamveka ngati ya nkhumba sizimasiyana.

2. Armin Meiwes wa ku Germany yemwe anadya nyama ya munthu, bambo wa zaka 43 mu chaka cha 2001. Iye anati nyama ya munthu imakoma chimodzimodzi ya nkhumba chabe imalimbirako kuyerekedza ndi ya nkhumba yo.

SIDENOTE
M***a kupanga google Armin Meiwes muzionere nokha zomwe ananena after kudya nyama ya munthu.

01/06/2026

Ati ku Dowa kwachitikaso chani abale 🤣🤣🤣 kufera pamwamba si wakugahena basi ?

Address

Mzuzu

Telephone

+265997782197

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when New Music posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to New Music:

Shortcuts

Share