Mintchana

Mintchana Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mintchana, Blantyre.
(11)

Welcome to Mintchana Page🎬
Home of fun, creativity, and entertaining content. 🀣🀣
Follow and enjoy the vibes! πŸ˜„
"Creating Smiles Through Content.”
I love you Lord ❀️πŸ₯°πŸ™Œ

20/05/2026

Vuto mukukonda Munthu oti mukacedza amakhala Watsegula chat yanuyo mwangozi nde mukuganiza zingayende?? πŸ’”πŸ’”πŸ€£πŸ€£πŸ™ŒπŸ™Œ

20/05/2026

Munadziwa liti kuti munthu sayamika??

20/05/2026

Tawelengani Mateyu 7 chapter chonsecho kenako munene zomwe mwaphunzirapo ndipo wina wamwayi atuluka ndi Mdalitso πŸ™πŸ™

Uthenga wachisoniWazimangilila kunyumba ya bwenzi lakeMtsikanayu dzina lake linali Mada. Malingana ndi ma lipoti, koyamb...
20/05/2026

Uthenga wachisoni

Wazimangilila kunyumba ya bwenzi lake

Mtsikanayu dzina lake linali Mada. Malingana ndi ma lipoti, koyamba atayambana ndi chibwezi chake chomwe ndi wa polisi anamwa mankhwala, koma mwamwayi anapulumutsidwa ndi anthu omwe anali pafupi naye ndipo sanamwalire.

Dzulo atapita kwa chibwezi chake, zikumveka kuti panali kusamvana ndipo chibwezi chake chinamusiya yekha m’nyumba n’kuchokapo. Tsoka ilo, chibwezicho chitabwerera usiku dzulo, chinapeza Mada atadzimangirira kale mnyumbamo ndipo anamwalira. πŸ™ŒπŸ™Œ

20/05/2026

😭😭😭 ndakhuzikika nditaona ma Comment pa post yomwe ndinanena kuti tigawirane ndalama ija wina ndi nzake πŸ˜­πŸ˜­πŸ’”πŸ’”πŸ™Œ Eish anthufe tisamangoonana tikaika ma pa picture abwino pa profile koma tikudutsa muzowawa πŸ™ŒπŸ™Œ

Choncho ndaganiza kuti tiyambe anthufe kuthandizana wina ndi nzake ndipo ziwani kuti kuthandiza sizitengera kuti Munthu ukhale nazo zambiri ayi koma ungokhala ndi mtima opeleka basi πŸ™ŒπŸ™Œ

Ambuye atisogolere πŸ™ŒπŸ™Œ

Congratulations Bayana Chunga (Angoni Wawo) , waphsa wa ku embassy  ku JapanπŸŽ‰
20/05/2026

Congratulations Bayana Chunga (Angoni Wawo) , waphsa wa ku embassy ku JapanπŸŽ‰

Nkazi uyu akufuna Mamuna iyeyo ati sanakhaleko pa banja alibeso mwana. πŸ€”πŸ˜˜
20/05/2026

Nkazi uyu akufuna Mamuna iyeyo ati sanakhaleko pa banja alibeso mwana. πŸ€”πŸ˜˜

20/05/2026

Amene sakuziwa kuti lero adya chani tanenani ku comment section. Ndipo achifundo tiyeni tithandize omwe akuonekadi kuti athodwa πŸ™

20/05/2026

Taikani chithunzi muli mu Jersey ya Arsenal kuti tione kuti mulipo angati.

Lero mpamene taona m’ma status mu kuti ndinuso a Arsenal🀣🀣πŸ”₯
20/05/2026

Lero mpamene taona m’ma status mu kuti ndinuso a Arsenal🀣🀣πŸ”₯

20/05/2026

Nzanga ukuwelengawe wadzuka bwanji kumeneko??

Address

Blantyre

Telephone

+265990464968

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mintchana posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Mintchana:

Share

//iconSize: [32, 32], //html: '' }) .bindTooltip(name, { //permanent: true, direction: 'bottom', //offset: L.point(12, 25), //opacity: 0.88, interactive: true }) .bindPopup(name); markersLayer.addLayer(marker); } function getMore() { if (gettingMore) { return; } gettingMore = true; var center = map.getCenter(); $.ajax({ url: "/vicinitysearch", data: { lat: center.lat, lng: center.lng, country: "MALAWI" } }) .done(function(data) { var added = 0; data.forEach(function(loc) { if (!locationIds.includes(loc.id)) { var mapLoc = {id:loc.id,lat:loc.latitude,lng:loc.longitude,title:trunc20(loc.name),popupHtml:loc.popupHtml,urlPath:loc.urlPath,pictureUrl:loc.pictureUrl}; locations.push(mapLoc); locationIds.push(loc.id); map._addMarker(mapLoc); added++; } }); }) .always(function() { gettingMore = false; }); } map._clearMarkers = function() { markersLayer.clearLayers(); } }); }, 4000); });