Tchooooo waves

Tchooooo waves I can't discover what everyone knows

22/10/2025

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Lalsan Lxr, Vinoth Raj, Mike Buleya, Emerson Masasa Jr., Luso Mulibe, Hermes Owen, Owen Stazio, Çhàñçy Lñx, Patience Manda, Deh-Kaputez Chimzy, Ken Davidson, Joe Noxy, Francis John FJizzy

   Ma model omwe avuta chaka chino.
12/10/2025




Ma model omwe avuta chaka chino.

   Malawi ntchito ikugwilaMzungu akadalemerabe 😂😂
11/10/2025




Malawi ntchito ikugwila
Mzungu akadalemerabe 😂😂

11/10/2025




Yavuta ndi awuvele fungo
Naneso nyimbo ndi yanga ndinalemba ndine 😂😂

07/10/2025




If January to December is 12 months
So why December to January is 1 month??? 🤔🤔

   MASO AWARD NOMINATIONS NOW OPEN! Maso Awards nomination are now open and will run till 25 October. Only one entry(vot...
07/10/2025




MASO AWARD NOMINATIONS NOW OPEN!
Maso Awards nomination are now open and will run till 25 October. Only one entry(vote) per category.
Let your voice be heard!

https://maso-awards.live/nominate

   US-based scientists John Clarke, Michel Devoret and John Martinis won the 2025 Nobel Prize in Physics for “experiment...
07/10/2025




US-based scientists John Clarke, Michel Devoret and John Martinis won the 2025 Nobel Prize in Physics for “experiments that revealed quantum physics in action”, paving the way for the development of the next generation of digital technologies

   Nkhani yavuta ndi ya beat. Onse akuti anaba. Palibe anagula🔥
07/10/2025




Nkhani yavuta ndi ya beat. Onse akuti anaba.
Palibe anagula🔥

    Mwambo olumbiritsa wachiwiri kwa wachiwiri wa mtsogoleri wa dziko lino a Enock Chihana, nduna zitatu komanso akuluak...
07/10/2025




Mwambo olumbiritsa wachiwiri kwa wachiwiri wa mtsogoleri wa dziko lino a Enock Chihana, nduna zitatu komanso akuluakulu ena a boma omwe mtsogoleri wadziko lino wawasankha uchitika mawa Lachitatu.

Mmodzi mwa akuluakulu ku ofesi ya mtsogoleri wadziko ndi nduna Dr. Maxwell Tsitsi watsimikiza izi mu kalata yomwe watulutsa lero ndipo wati mwambowu ukachitikira kunyumba ya prezidenti Mutharika ku Nyambadwe.

(by Broxter -Blantyre:10/07/2025)

  Oyendetsa galimoto yonyamula odwala  (Ambulance ) pa chipatala chachikulu cha m'boma la Ntchisi a Kondwani Kamawanga a...
07/10/2025



Oyendetsa galimoto yonyamula odwala (Ambulance ) pa chipatala chachikulu cha m'boma la Ntchisi a Kondwani Kamawanga azaka 48 avulala ndipo agonekedwa pachipatalapo potsatira ngozi yomwe yachitika m'bandakucha wa lero.

Mneneri pa chipatalapo a Frank Kaphaso komanso ofalitsa nkhani za apolisi m'bomalo a Salomy Zgambo atsimikiza za ngoziyi.

Polankhula ndi Tchooo Waves mchipinda chomwe awagoneka a Kamawanga ati pa nthawiyo amachokera kotenga odwala ku chipatala chaching'ono cha Kangolwa ku dera la Mfumu yaikulu Kasakula m'bomalo.


(by Odniz Zindo -Ntchisi:06/10/25)

   Pali mpungwe pungwe pakati pa TeamOnesimus ndi Team Merchah.Pa nkhani ya beat yomwe oyimba awiliwaIkufanana ndi nyimb...
07/10/2025




Pali mpungwe pungwe pakati pa Team
Onesimus ndi Team Merchah.
Pa nkhani ya beat yomwe oyimba awiliwa
Ikufanana ndi nyimbo zawo atulutsa chakumene.
More in comment section 🔥

Address

Ntchisi

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Tchooooo waves posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share