Anganya Roots Frequency.

Anganya Roots Frequency. Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Anganya Roots Frequency., Arts and entertainment, Nkhotakota.

Kwa amgomba adabwa nazo kuti mchezo wanji kongonveka chamba chokhachokha thobwa kulibeso.
21/08/2026

Kwa amgomba adabwa nazo kuti mchezo wanji kongonveka chamba chokhachokha thobwa kulibeso.

Panthawi yayitali, akaka nkoyamba Nkhotakota kupanga chinthu ngati ichi. Kuyambira pomwe swed cup inayambira ndipomwe le...
21/08/2026

Panthawi yayitali, akaka nkoyamba Nkhotakota kupanga chinthu ngati ichi. Kuyambira pomwe swed cup inayambira ndipomwe lero tayimaliza, zangowonetsa kuti chidwi cha mpira wa miyendo komaso wa manja kwathu kuno chiliko zimangosowa otiyambitsira.

Tithokonze bwana Ibrahim Swed ndi ena omwe anatenga nawo mbali potiyanjanitsa ndikubweretsa chisangalaro pakati pathu ndipo tikuyembekezeraso kuti chaka chamawa izizi zizachitikeso. Pamene chikhochi chatha ndi 4 - 2 . Tasangalala ndipo tsiku la relo latha likukoma.

Zimangotengera imene imakuwazayo koma izizi zilibe maudolo magaye. Well tiyambe nchito zathu.
21/08/2026

Zimangotengera imene imakuwazayo koma izizi zilibe maudolo magaye. Well tiyambe nchito zathu.

Uncle Ibrahim Swed awonetsa pangolin amene akatenge opambana pa cup yomwe anakhazikitsa pa masewero ampira wa manja tiye...
20/08/2026

Uncle Ibrahim Swed awonetsa pangolin amene akatenge opambana pa cup yomwe anakhazikitsa pa masewero ampira wa manja tiyeni anganya mawa pa 21 August 2026 (Friday) pa St Pauls ground pamene tikachitile umboni pakati pa sensi Kms hot killers akuitenga chinthuchi

Anganya  dirty wathu wathu uyu mumpasa like abale alowe mkati ,, mario bro Boma ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚
20/08/2026

Anganya dirty wathu wathu uyu mumpasa like abale alowe mkati ,, mario bro Boma ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

Anganya  ma set kukonzekela Ku finals ya Ibrahim Swed cup pa 21 August Pano๐Ÿ˜‚
19/08/2026

Anganya ma set kukonzekela Ku finals ya Ibrahim Swed cup pa 21 August Pano
๐Ÿ˜‚

Airtel Malawi ndi TNM (Telekom Networks Malawi)   Mukanangotiuza kuti bundleyi ndi yogwiritsira ntchito kuona ma message...
17/08/2026

Airtel Malawi ndi TNM (Telekom Networks Malawi) Mukanangotiuza kuti bundleyi ndi yogwiritsira ntchito kuona ma message pa whatsapp. Ndife anthu onvetsetsa tikanakunverani.

Pa 21 August 2026 pa st pauls ground Nkhotakota patelera Ibrahim Swed cup finals Afana Vs Mpondagaga Sens Vs HotkillersP...
16/08/2026

Pa 21 August 2026 pa st pauls ground Nkhotakota patelera Ibrahim Swed cup finals
Afana Vs Mpondagaga
Sens Vs Hotkillers
Pa tsikuli kuzakhala BLACK MISSIONARIES kusangalatsa anthu ,,tikakhala ife nde tizakhala konko stingaphonye

14/08/2026

zeronine
nyenyezi coming soon.....๐Ÿšจ๐Ÿšจ๐Ÿ“ข

Sitikukukakamizani komano mukanakwatira ndikale lija ๐Ÿ˜ฎโ€๐Ÿ’จ
14/08/2026

Sitikukukakamizani komano mukanakwatira ndikale lija ๐Ÿ˜ฎโ€๐Ÿ’จ

Address

Nkhotakota

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Anganya Roots Frequency. posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share