Asumi Entertainment

Asumi Entertainment Asumi is Entertainment platform for Neno. Bridging talent, entertaining, news updates, health talk, crazy facts and jokes is what it's all.

Photos, Videos and GIF posted here are that are social media

22/08/2026

Happy Sabbath abale ndi alongo..

Lero mwati tikapemphera kuti?..

Zikuchitika mwa Chinsisi tu. utha kungopeza watsala wekha, anzako akwatira. Congrats Brother Martin
21/08/2026

Zikuchitika mwa Chinsisi tu.
utha kungopeza watsala wekha, anzako akwatira.
Congrats Brother Martin

Chochitika Sunday chapezeka...tiyeni tiwapatse molaro anyamata athu...k1000 pa gate...p***a pa Neno stadium
21/08/2026

Chochitika Sunday chapezeka...

tiyeni tiwapatse molaro anyamata athu...

k1000 pa gate...

p***a pa Neno stadium

18/08/2026

wapanga 50 pin Lero ndimamuna.. eeeeee kunja kwauma uku.....

mchifukwa chake ena amangokhwima.. eish

18/08/2026

Morning neba!!

Tsiku loti ulemere limacha ngati tsiku lililonse...

Mwina Lero ndi lako....
tiye tikayesenso

Bwalo la Ndege hilltop. Next time mudzatitengeMutsambamy nso tiyendeno bola Zazokwanira basi
18/08/2026

Bwalo la Ndege hilltop.
Next time mudzatitenge
Mutsambamy nso tiyendeno bola Zazokwanira basi

Ngakhale kwazizira.... komabe mwambo sungalephereke.....
15/08/2026

Ngakhale kwazizira.... komabe mwambo sungalephereke.....

15/08/2026

Neno district imodzi MWA ma district omwe tapala kwambiri Mayeso a 8 and form 2....

Neno and Nsanje the worst performing districts..

AYI ZIKOMO

15/08/2026

Machine wo asowa bwanji pa chipatala....

Kuseweratu ndi moyo WA patient uku..

adatilodzayo ndi mfitidi

Lero kwachera iziJust InThe Malawi National Examinations Board (MANEB), in conjunction with the Ministry of Education, S...
15/08/2026

Lero kwachera izi

Just In

The Malawi National Examinations Board (MANEB), in conjunction with the Ministry of Education, Science and Technology, has released the 2026 Primary School Leaving Certificate of Education (PSLCE) and Junior Certificate of Education (JCE) examination results.

A total of 245,048 candidates sat for the PSLCE, with 198,903 passing, representing an 81.17 percent pass rate.

For the JCE, 125,777 out of 154,880 candidates passed, representing an 81.21 percent pass rate.

Address

Neno
NONE

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Asumi Entertainment posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Asumi Entertainment:

Shortcuts

Share