Nyaxy

Call Directions Website

Nyaxy We here to pick up the world

08/08/2026

Not everything you desire is what you require.
Be grateful for Life & good Health✌️ @

Bungwe loyendetsa masewelo a mpila wa miyendo la dziko la Uganda lalengeza kuti osewela wa timu ya SC Villa amene anabay...
08/08/2026

Bungwe loyendetsa masewelo a mpila wa miyendo la dziko la Uganda lalengeza kuti osewela wa timu ya SC Villa amene anabayidwa ndi achifwamba Issac owori David wamwalira.

Owori anakumana ndi achifwamba nthawi imene amapita kunyumba kwake usiku wa dzulo amene anamutema ndizikwanje.

Iyeyu anali mtsogoleli wa timu ya SC Villa kapena kunena kuti Captain pa chingelezi komaso amatumikila timu ya dziko lake.

Source :FUFA & Eddy Kenzo olemba nyaxy 🆕s like and share

Osewela wa timu ya Sv werder bremen ku Germany Karim coulibaly ali manja mkhosi pamene wapeza kuti akuba amuimitsila gal...
08/08/2026

Osewela wa timu ya Sv werder bremen ku Germany Karim coulibaly ali manja mkhosi pamene wapeza kuti akuba amuimitsila galimoto yake pamwamba pama block a cement ndipo matayala onse 4 amubela kucha kwa dzulo .

Xabi Alonso's Chelsea continued their pre-season preparations with a 3-0 win over Ruben Amorim's AC Milan ⚽️🔵
08/08/2026

Xabi Alonso's Chelsea continued their pre-season preparations with a 3-0 win over Ruben Amorim's AC Milan ⚽️🔵

Address

Mzuzu

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nyaxy posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share