Mphenipo

Mphenipo Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mphenipo, Arts and entertainment, Mzuzu.

11/05/2023

Pamene ine ndimafika ndinapeza Bee jay akumuuza mtolankhani wa otchedwa Henry Czar k*t bwanji asamulipilitse nkhani zakezo kma amupatse ulure. Kma Giboh Pearson Phalombe Musik mwa ndi wake anangofika mokuwa amvekere "USAMUPASE NDI MPASA" Anthu tonse pakamwa kakasi😔

09/03/2023

Kell Kay just adopt me plz 😊 olo ngat zilizovuta basi tizakhala opuputa PS

Abwana awa mukava ndawagenda musandiiimbe mulandu coz akundiyambira dala 😎GGwambamumafuna ghetto izivera chani
08/03/2023

Abwana awa mukava ndawagenda musandiiimbe mulandu coz akundiyambira dala 😎

GGwambamumafuna ghetto izivera chani

08/03/2023

Mr Gwamba ngat simutulusa nyimbo mwezi uno muziyenda chewuchewu chifukwa nde kumene kuzachoke mwala simazakuziwa bhobho😎😎

08/03/2023

Kod Ras EvanzMuzik zomwezi mpaka tizagende😎

08/03/2023

Kod Kell Kay sungangoyimbeso nyimbo zina 4 k*ti ungotimalizilatu😀 sinanga mwatiyamba dala nokha potulusa hit ngat imeneyi😊

08/03/2023

Ngat sumamufila Kell Kay that's ur 😊 Wataya makina😝😀

03/03/2023

Kod Gwamba zomwezi mpaka tizagende

03/03/2023

Kma amwene Charisma Madness nyimbo ija mwayipwetekadi mmmmm ndimayimvera kumaloto kma eeeee braza ituluseni mawa lomweli basi😊

08/02/2023

Perfume sanukha kanthu kwa nunkha dala/
Usalimbane ndimafana okula opanda madala/💪💪😊

KAPKAPADOCIA

Address

Mzuzu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mphenipo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share