MRI Gospel POEMS

MRI Gospel POEMS Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from MRI Gospel POEMS, Poet, Mzuzu.

02/01/2023

Poem by MVULA Lightwell; tittled; akazabweranso kachiwili. Akazabweranso kachiwili,mapili adzagwedezeka
Mphepo yamlenga-lenga idzanthunthumila
Ndikuthuluma kooosa ndimkeiyo wogadima kuxhoka m'maso mwake
Anamvachifundo muulendo woyambayo
atakuyang'anani atandiyang'ana atawayang'ana
Chifundo chofa nacho chinam'chondelela
Ndizolengedwa zikagwedezeka momunyadila
Mbalame zinayimba zachifundo chake pomwe munthu sadalingalile

Tizadzidzimuka ndimilili yazilango akazabweranso kachiwili,mosaumila lupanga take ntchito idzapanga,
Kuotha Moto kuzakhala kosathawidwa,
Evola Hlv ndi ntchenga, anabwela ngati coming kuzachenjeza uthenga, koma kufuna keake sitipanga,mundende yakumdima mtima wathu tidamana kujomba kumapemphelo ndiye kosayamba
,Zamasewelo Zili thafya m'miti.a kutenga Malo ake sitimanga may ake pamtima ku buloka lonjezano lake
Akazabweranso kachiwili
Sipazakhala discount
Kunjako ukhrist tauponya patchuti nyasi ndizokhumudwitsa woyelayo zabalalika
Zothawa m'busa nkhosa tasanduka tizagomoka ngati sodomu ndi gomola
Nthawi yayandikila
Tsoka lofuna lizatiopsa
Kadaziwa sikadapanga uzakhala mwambi
Anayamba ndikutiwona ndichifundo koma pano tizawona Moto ngati womwe adawona mose koholebi
Zizachitika
Akazabweranso kachiwili 🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏

Address

Mzuzu

Telephone

+265995038761

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MRI Gospel POEMS posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category