Vizzier Ngwira

Vizzier Ngwira TUMBUKA KINGDOM πŸ”₯πŸ₯΄

24/08/2026

KUTIBELA NDALAMA DZIKO NGATI AGENT πŸ˜«πŸ™„

KHUDA WACHOKA KU MASTERSKatswiri wosewera kutsogolo mu timu ya Masters FC Khuda Muyaba wachoka kutimuyi kutsatira kumvan...
04/08/2026

KHUDA WACHOKA KU MASTERS

Katswiri wosewera kutsogolo mu timu ya Masters FC Khuda Muyaba wachoka kutimuyi kutsatira kumvana kwa mbali ziwirizi kuti zitero.

Malingana ndi mmodzi mwa olemba nkhani mdziko muno Twaha Chimuka, Muyaba samagwirizana ndi mphunzitsi Peter Mponda koma timuyi yati ili mbali ya mphunzitsi wawo ndipo yemwe sakugwirizana naye achoke ndi iyeyo.

Ndipo Katswiriyu akhale akubwenza ndalama zomwe anatenga atasaina mgwirizano wake kutimuyi kutsatira zomwe onse agwirizana.

Muyaba anapita ku Masters masabata atatu apitawa ndipo wangoseweratu masewero awiri okha ndi kuthandizira zigoli ziwiri komanso kutenga mphoto ya osewera wapamwamba pa masewero kamodzi.

Source : Twaha Chimuka.
NB. copied

awa mpira uwavutaaaa khalidwe mulibe mxiew πŸ™„
04/08/2026

awa mpira uwavutaaaa khalidwe mulibe
mxiew πŸ™„

EEE MPAKANA PHAZI πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚
22/07/2026

EEE MPAKANA PHAZI πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

EKWENDENI-MZIMBA PANTHU APA III πŸ˜…
18/07/2026

EKWENDENI-MZIMBA
PANTHU APA III πŸ˜…

Now listening  Trinket TeeChannel   No silence ..🀫🀫🀫
25/06/2026

Now listening Trinket TeeChannel
No silence ..🀫🀫🀫

29/05/2026
hipapu IKK  get well soon🐐
29/05/2026

hipapu IKK get well soon🐐

PANO ZAFIKA KUMENYA..... I HOPE ZAMVEKA πŸ˜‚πŸ˜‚
27/05/2026

PANO ZAFIKA KUMENYA.....
I HOPE ZAMVEKA πŸ˜‚πŸ˜‚

Address

Ekwendeni Mzimba
Mzuzu

Telephone

+265887301868

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Vizzier Ngwira posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Vizzier Ngwira:

Shortcuts

Share