Poethassa Tembo

Poethassa Tembo Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Poethassa Tembo, Poet, Kasungu, Mzuzu.

27/04/2023

From driemo akut thanks

27/04/2023

Sanje siimanga mudzi Driemo nyimbo zake zonse ma million views God bless you nyimbo ikhale mojo mmawa Uno❤️❤️❤️❤️

19/02/2023

Pali mwambi uwu amati, 'Mphechepeche mwa njobvu sadutsa kawiri'

Koma olo koyambako komweko uzidutsa nkumati ukupita Kuti?

😂😂😂😂😂😂😂

Mlamu wanga wakale wakutumula yanyowani uku,,,,Eya paja amati chiLAMU sichithatu. 🤣🤣🤣. Koma Musamakhale amabodza apa.Whe...
19/02/2023

Mlamu wanga wakale wakutumula yanyowani uku,,,,Eya paja amati chiLAMU sichithatu. 🤣🤣🤣. Koma Musamakhale amabodza apa.
Whenever you coming up with some good stuff tilipano kukubweretserani.
Here's new tune from JayJay Jay Cee MwyJay Jay Cee MweJay Jay Cee Mw Jay Jay Cee Mwinda
https://www.adzukulu.com/songs/jay-jay-cee-mw-linda-pamodzi-album/
*16✓
🙏

19/02/2023

Vep atha kukuchotsa koma Skill Sangakubele 🙏

19/02/2023

Ndalama olo usamwere mowa imathabe...

19/02/2023

Anthu mwafatsatu, mukungoyang'ana zomwe zikuyendayenda ndikupitapita mudziko.

19/02/2023

Tchulani Mzanu Amene Akuoneka Kuti Wakula Akufunika Akwatire 😂😂😂
No mercy!

19/02/2023

SUNDAY MORNING VERSE ( Yesaya 54:4 )

"Usachite mantha; sadzakunyozanso. Usakhumudwe; sudzapeputsidwanso. Udzayiwala za manyazi zimene zinakuchitikira nthawi ya unyamata wako ndipo za manyazi zimene zinakuchitikira pa nthawi ya umasiye wako sudzazikumbukanso "

GOODMORNING ☀️

19/02/2023

Tchulani mzanu m'modzi wamakani kwambiri oti olo Kumwamba atha kukayambana ndi Angelo!

19/02/2023

Bola inu mwanva kukoma lero, koma Ife timangonvera zinatha kuseliku,💔 ayi Zikomo🙏

Address

Kasungu
Mzuzu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Poethassa Tembo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category