GOD POWER MEDIA

GOD POWER MEDIA BIBLE STUDY
CHOLINGA CHANGA NDI
2 Timoteyo 3:16
othandiza pophunzitsa, podzudzula, pokonza cholakwika ndi polangiza za chilungamo
(3)

NDE KULI UYU AMATI Morton Baghaya KUMAPANGA BACK ZINTHU ZOPUSA😪ZOTI MUZIYIPISA DZINA LA MULUNGU MMM MUZINGOCHIMWIRAPO AP...
04/05/2026

NDE KULI UYU AMATI Morton Baghaya KUMAPANGA BACK ZINTHU ZOPUSA😪
ZOTI MUZIYIPISA DZINA LA MULUNGU MMM MUZINGOCHIMWIRAPO APA POMWE PALAKWIKA PLZ DZUDZULAN OSABAKIRA USILU AYI, UYU MIRACLE VIC CHING UYU PANO KUNENADI ZAOONA PA GOSPEL ANATCHOKAPO CHIFUKWA NYIMBO ZAKE NDI KHALIDWE LOMWE AKULIONESA ZOSIYANA KUTALI CHIFUKWA MAU AKUTI

1 Timoteyo 2:9
Ndikufunanso kuti amayi azivala mwaulemu, modzilemekeza ndi moyenera. Adzikongoletse koma osati ndi tsitsi loluka mowonjeza muyeso kapena zokongoletsa zagolide kapena mikanda yamtengowapatali kapena ndi zovala zamtengowapatali.
1 Timoteyo 2:10
Koma adzikongoletse ndi ntchito zabwino zoyenera mayi wopembedza Mulungu.

NDE ALIYESE AMENE AKUBAKIRA ZINTHU NGATI IZI IYESO AMAKHALA MUZOMWEZO
ZIKOMO
MUUZENI UYU MULUNGU SI DZINA LOLISEWERESA
🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏

03/05/2026

Tilipo angati womwe tazuka ndi moyo pano changu tangolemba ambuye zikomo

🔥 UNENERI WAMPHAVU LERO 🔥Monga mmene zalembedwera pa Marko 5:27-29…Mkazi uja anangokhudza chovala cha Yesu, ndipo nthawi...
02/05/2026

🔥 UNENERI WAMPHAVU LERO 🔥

Monga mmene zalembedwera pa Marko 5:27-29…
Mkazi uja anangokhudza chovala cha Yesu, ndipo nthawi yomweyo anachira!
Lero ndikulengeza pa moyo wako: Kukhudza kumodzi kwa Mulungu kusintha nkhani yako yonse!
👉Wakhala ukufuna business Lero Mulungu akupatse chifukwa sanakulenge ovutika
👉 Ululu wako usanduka chimwemwe
👉 Matenda achoke, pa nthupi lako ndipo machiritso abwere
👉 Chilichonse chimene umaona Kuchedwa kusinthe kukhala mwachangu
👉Iwe banja likumakuvuta kukhazikika Lero ndikulengeza kuchotsa ka mzimu kosakhazikika pa Banja,
👉Yehova mwini zonse achotse zamatsenga zonse zimene amakupangirani zija mu dzina la yesu.

🔥 Zaka zomwe wataya zibwezeretsedwa!
🔥 Misozi yako isanduke umboni!
Palibe chimene chili chovuta kwa Mulungu!
Lero ndi tsiku lako losintha… MU DZINA LA YESU! 🙏

“AMEN” pansipa!Ndikulengeza pa anthu 4000 Malo ano before madzulo wano Mulungu abwelese chimwemwe pa moyo wanu (John 11 vs 44).

AMEN AMEN MULUNGU AKUDALITSENI INU NONSE MULI NDI CHIKHULUPILIRO MWA AMBUYE
FOLLOW POWER MEDIA
WITH Denzo Mo Sakuwa

02/05/2026

Ukapanga @ amene abwere pa number 3 uyo Lero weekend akugulira bundle, tiyeni

NKHALANI A CHIKHULUPILIRO PA MULUNGU NGATI YOBUŴaHebere  10 : 23Tikoreske chipulikano chithu icho tikuzomera, pakuti Chi...
01/05/2026

NKHALANI A CHIKHULUPILIRO PA MULUNGU NGATI YOBU

ŴaHebere 10 : 23
Tikoreske chipulikano chithu icho tikuzomera, pakuti Chiuta uyo wakachita phangano ili, ngwa kugomezgeka.
Miyambo 3:3
Makhalidwe ochitira ena chifundo ndi owonetsa kukhulupirika asakuchokere. Uwamangirire mʼkhosi mwako ngati mkanda ndi kuwalemba pa mtima pako.

Ahebri 10:22
Tsono tiyeni tiyandikire kwa Mulungu ndi mtima woona ndi wodzaza ndi chikhulupiriro. Popeza mitima yathu yayeretsedwa, ndi yopanda chikumbumtima chotitsutsa, ndiponso matupi athu asambitsidwa ndi madzi woyera.

Ahebri 10:23
Tiyeni tigwiritsitse mosagwedezeka zimene timaziyembekezera ndi kuzivomereza, pakuti amene anatilonjezayo ndi wokhulupirika.

Ahebri 10:24
Tiziganizira mmene tingalimbikitsirane wina ndi mnzake pokondana ndi kuchita ntchito zabwino.

FOLLOW GOD POWER MEDIA WITH Denzo Mo Sakuwa
MULUNGU AKUDALITSENI INU NONSE HALLELUJAH
🌷🌷🌷🌷🌷🌷🌷🌷🌷🌷🌷🌷🌷🌷

30/04/2026

Lelo lomweli zuwa lisanalowe Mulungu akhala atasitha nyengo zako iwe ukuwelenga🙏

NKHAWA ZANU TAYANI PA YESU KHRISTU NDIPO AZAKULANDIRANI Mateyu 11:28“Idzani kwa Ine, inu nonse otopa ndi olemedwa ndipo ...
30/04/2026

NKHAWA ZANU TAYANI PA YESU KHRISTU NDIPO AZAKULANDIRANI

Mateyu 11:28
“Idzani kwa Ine, inu nonse otopa ndi olemedwa ndipo Ine ndidzakupatsani mpumulo.
Mateyu 11:29
Senzani goli langa ndipo phunzirani kwa Ine, pakuti ndine wofatsa ndi wodzichepetsa. Ndipo inu mudzapeza mpumulo wa miyoyo yanu.
Mateyu 11:30
Pakuti goli langa ndi losavuta ndipo katundu wanga ndi wopepuka.”Miyambo 12:25
Nkhawa imakhala ngati katundu wolemera mu mtima mwa munthu, koma mawu abwino amamusangalatsa.

1 Petro 5:7
Tayani pa Iye nkhawa zanu zonse chifukwa ndiye amakusamalani.

Follow WITH BROTHER WANU Denzo Mo Sakuwa

29/04/2026

Mlaliki 10:2
Wanzeru, mtima wake uli kudzanja lake lamanja; koma chitsiru, mtima wake kulamanzere.

NDE KULI A Prophet Austin LiabunyaKUMAWANAMIZA ANTHU 🙄🙄🙄1 Yohane 4:5Aneneri onyengawa ndi ochokera mʼdziko lapansi, nʼch...
29/04/2026

NDE KULI A Prophet Austin Liabunya
KUMAWANAMIZA ANTHU 🙄🙄🙄
1 Yohane 4:5
Aneneri onyengawa ndi ochokera mʼdziko lapansi, nʼchifukwa chake amayankhula za dziko lapansi, ndipo dziko lapansi limawamvera.

MAU AKUTI CHANI
Levitiko 19:27
“ ‘Musamamete mduliro mutu wanu, kapena kumeta mʼmphepete mwa ndevu zanu.
SO CHECK A PROPHET ANUWA👁️
Mateyu 24:24
Chifukwa akhristu onama ndi aneneri onama adzaoneka ndipo adzachita zizindikiro zazikulu ndi zodabwitsa kuti akanyenge ngakhale osankhidwawo ngati kukanakhala kotheka kutero.
Mateyu 24:25
Onani, ndakuwuzani izi nthawi isanafike.
Mateyu 24:26
“Ndiye ngati wina akuwuzani inu kuti, ‘Uyo ali ku chipululu,’ inu musapiteko; kapena akati, ‘Uyu ali kuno mʼchipinda chamʼkati,’ musakhulupirire.

Address

Mzimba

Telephone

+265887096964

Website

https://youtube.com/@denzomosakuwa-kg6lm?si=ldEEGb5QHdz77kka

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when GOD POWER MEDIA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to GOD POWER MEDIA:

Share

//iconSize: [32, 32], //html: '' }) .bindTooltip(name, { //permanent: true, direction: 'bottom', //offset: L.point(12, 25), //opacity: 0.88, interactive: true }) .bindPopup(name); markersLayer.addLayer(marker); } function getMore() { if (gettingMore) { return; } gettingMore = true; var center = map.getCenter(); $.ajax({ url: "/vicinitysearch", data: { lat: center.lat, lng: center.lng, country: "MALAWI" } }) .done(function(data) { var added = 0; data.forEach(function(loc) { if (!locationIds.includes(loc.id)) { var mapLoc = {id:loc.id,lat:loc.latitude,lng:loc.longitude,title:trunc20(loc.name),popupHtml:loc.popupHtml,urlPath:loc.urlPath,pictureUrl:loc.pictureUrl}; locations.push(mapLoc); locationIds.push(loc.id); map._addMarker(mapLoc); added++; } }); }) .always(function() { gettingMore = false; }); } map._clearMarkers = function() { markersLayer.clearLayers(); } }); }, 4000); });