CLUB 265

Directions

CLUB 265 Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from CLUB 265, Arts and entertainment, Mponela.

08/08/2026

ZIFUKWA 20 ZOMWE BIZINESI ZAMBIRI KU MALAWI SIZIKULA

1. "BOLA TIKUDYA" MINDSET (SURVIVAL MENTALITY)
Anthu ambiri amangofuna ndalama zokwanira kudya lero. Saganizira za growth, expansion, kapena legacy. Bizinesi yabwino siyimangokupatsa chakudya cha lero, imamangidwa kuti izithandiza banja ngakhale zaka zambiri zikubwera. Allah akunena kuti tipemphe zabwino zake (Qur'an 4:32), choncho kulakalaka kukula sikuli umbombo.

2. Kudya Capital M'Malo Mwa Profit
Capital ndi mtima wa bizinesi. Ngati mukudya ndalama zogulira katundu, bizinesi imangozungulira osakula. Protect your capital. Muzidya profit, osati capital.

3. KUSABWEZERETSA PROFIT (NO REINVESTMENT)
Profit ikabwera, gawo lina liyenera kubwerera mubizinesi. Reinvestment ndiyo mafuta a kukula kwa bizinesi. Popanda izi, kukula kumachedwa kwambiri.

4. KUSASIYANITSA BUSINESS MONEY NDI PERSONAL MONEY
Ndalama za shop siziyenera kukhala ndalama za kunyumba. Tsegulani separate account kapena bokosi lapadera la bizinesi. Mukasakaniza ndalama, simudzadziwa ngati mukupindula kapena mukutaya.

5. KUSASUNGA MA RECORDS (POOR RECORD KEEPING)
Ngati simulemba sales, expenses, stock, ndi profit, mumangoyendetsa bizinesi ndi malingaliro. What gets measured gets improved.

6. KUSOWA BUDGET
Bizinesi yopanda budget imawononga ndalama mosaganizira. Konzani ndalama za mwezi uliwonse musanagwiritse ntchito.

7. KUGULA ZINTHU ZOKONGOLA Musanayime Bwino
Ena amagula galimoto, phone kapena zinthu za mtengo wapatali pomwe bizinesi sinakhazikike. Assets should produce income before buying luxuries.

8. BUSINESS YA MUNTHU MMODZI
Ngati zonse zimadalira inu, mukadwala kapena kuyenda, bizinesi imaima. Pangani systems, procedures, ndi kuphunzitsa antchito.

9. KUSAPHUNZIRA ZATSOPANO
Market imasintha nthawi zonse. Successful entrepreneurs never stop learning. Werengani mabuku, pitani kuma training, phunzirani pa intaneti, ifetu tikuphunzira pompano komanso tikuphunzitsa ena

10. KUSADZIWA CUSTOMER SERVICE
Makasitomala amabwerera chifukwa cha momwe mu

10/04/2026

kodi mukujama iti kwanuko?

Address

Mponela

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when CLUB 265 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share