Afana matrix

Afana matrix Dolo KanGapo

25/04/2025

Umugulire mkazi wako bra ndiye uyiwale kumupasa then azamupeze yekha 😅Malume nkhondotu😅🙌🏻

22/04/2025

🤔🤔😂

21/02/2025

zafika pok*ti ndondocha yokawa ikumabwela ikupukusa mutu eish🙌🙌

MORGAN  ATHERA MMANJA👇NEBA🥴: bwanji ukuoneka okhumudwa neba?MORGAN😉: nkhawa zanga ndizochuluka kwambiliNEBA🥴: bwanjiso n...
28/12/2024

MORGAN ATHERA MMANJA👇

NEBA🥴: bwanji ukuoneka okhumudwa neba?

MORGAN😉: nkhawa zanga ndizochuluka kwambili

NEBA🥴: bwanjiso neba? Tandiuze ulitu ngat bale wanga, moti vuto lako ndi vuto langaso

MORGAN🥴: ineyooo ndimafuna ntapemphako zinthu ziwili mundithandizire

NEBA🥴: ukufuna ngongole?

MORGAN😉: ayisooo, nkhani siyandalama

NEBA🥴: nde ukufuna ndik*thandizire chani?

MORGAN😉: nkhani yoyamba: mkazi Wa bambo wanga, yemwe ndi Mai anga,, sakundisangalatsa masiku ano

NEBA🥴: sakukusangalatsa motani? Mesa ndi Mai ako?

MORGAN😉: eya ndi Mai anga, kma dzulo nnali ku Bar inayake, eeeeh kuli zi akadzi zokongolaa. Zamatakooo mweneeeee

NEBA🥴: nde zugwilizana bwanji ndi Mai ako k*t asakusangalatse?

MORGAN😉: Ndikuona ngat bambo anga anapanga phuma pokwatira babe yaoyiii,,cz akanadekha bwezi Mai anga Ali achithakooo

NEBA🥴: iweyooo mmutumo nzeru mulibe,, zoona Mai ako ukafanizire ndi hule?

MORGAN😉: iiiih Bas zatha chabwino

NEBA🥴:nde nkhani inayoo umati bwa?

MORGAN😉: ndiyokhuza akazi anu.

NEBA🥴: akazanga atani?

MORGAN😉: muwauze k*t ngat 2025 akubwerayii matchajidwe a business yao akhale omwewaaa, ndikulumbiira chekecheke twaaaa sazalemera

NEBA🥴: pongo akazanga amapanga business?

MORGAN😉:eyaaaaa, mesa short time amapanga 600kwacha?

NEBA🥴: kd pongo uk*tii bwanji kd? Tandiuze bwino asee,, sono ukupitasooo k*t?

MORGAN😉: 🏃‍♂️🏃‍♂️🏃‍♂️🏃‍♂️iiiiih bola ndakuuzani k*t akazanu ndi huleeeeeeeee🗣️🗣️🗣️🗣️🗣️ muwauzeso k*t shaver ndi 500kwacha zaumve ayiii ma customer ifeeee sitifunaaa.

18/12/2024

Address

Monkey Bay

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Afana matrix posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share