Artworks Malawi

Artworks Malawi Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Artworks Malawi, Theatrical Productions, Mchinji.

Osayiwala kusamba mmanja  tikachoka malo ozithandizila, tisanadye tisambe mmanja, tikayambisa  ana tizisamba mmanja  tis...
13/01/2024

Osayiwala kusamba mmanja tikachoka malo ozithandizila, tisanadye tisambe mmanja, tikayambisa ana tizisamba mmanja tisananambe Ku phika tisambe mmanja, tizidya zakudya zophika tisamangogula zakudya mu musewu ndikudya kuti tipewe matenda a cholera

Artworks kutenga nawo gawooo  makamaka pa clean up exercise  yomwe  imachitikila pa Kamwendo    iwooo  ati ndichofunikil...
13/01/2024

Artworks kutenga nawo gawooo makamaka pa clean up exercise yomwe imachitikila pa Kamwendo iwooo ati ndichofunikila kwambiri kukoza mmadela athu komaso malo omwe timachitila malonda kuti tinkhale awunkhondo komaso tipewe cholera

Palibe chithu chofunikila ndichosangalatsa ngt  kukoza m dera lathu kukoza malo ogwirira ntchito  opangila  malonda anth...
13/10/2023

Palibe chithu chofunikila ndichosangalatsa ngt kukoza m dera lathu kukoza malo ogwirira ntchito opangila malonda anthu nditchito ya aliyese ngt Artworks inaona chithu chofunikila kutenganawo gawo
Lelo pa 13 October 2023 pa Mchinji Boma

Wapampando wa gulu LA Artworks Cecilia Nkhuwa komanso mlembi was gululi Prisca Phiri  ndiomwe anatenganawo mbari pa mwam...
25/08/2023

Wapampando wa gulu LA Artworks Cecilia Nkhuwa komanso mlembi was gululi Prisca Phiri ndiomwe anatenganawo mbari pa mwambowu
Ndipoiwooo akutsimikiza kutizomwe ava ndikuona kumwambowuzithandiza a gulu lawo kusitha ndikulinbikisa achinyamata posamala chilengedwe

District environmental officer Mr soko Lelo pa 25 August kuyankhulapo pamwambo omwe a GAYO anapangitsa maka onkhudza chi...
25/08/2023

District environmental officer Mr soko
Lelo pa 25 August kuyankhulapo pamwambo omwe a GAYO anapangitsa maka onkhudza chilengedwe .iwooo alimbikitsa achinyamata komaso kuwaunikila chomwe achinyamata Ali ponena kuti achinyamata alipo ochuluka ,alindi mphavu yongwira ntchito ,Ali ndi Thawi yositha zinthu maka pobwezeletsa chilengedwe
Ayamikila bugwe LA GAYO potsogolela mwambowu komaso ponkhala ndi chiganizo chopangitsa mwambowuuu

Social media campaign  tithokoze bugwe LA GAYO  potisankha kunkhala gulu lotengako gawoo. Kumwambo ofunikilawu
30/06/2023

Social media campaign tithokoze bugwe LA GAYO potisankha kunkhala gulu lotengako gawoo. Kumwambo ofunikilawu

March  ndimwezi omwe timakumbukila amayi onse  mmalo make mwambowu unachitika pa 11march pomwe  ARTSIKANA  malimbikisa a...
13/03/2023

March ndimwezi omwe timakumbukila amayi onse mmalo make mwambowu unachitika pa 11march pomwe ARTSIKANA malimbikisa atsikana omwe alindimaluso osiyanasiya kuti maso ankhale chitsogololo awooo pofuna kukwanilitsa maso phenya awoooo
Artworks ibatenga nawo gawo pa mwambowuuuu kuti unkhale okoma poobetsa sewero konaso ndakatulo
Linali tsiku lokoma kwambiri pomwe alendo ochoka Ku south Africa adayamikila ndikulimbikisa gulu LA artworks pa maluso omwe tilinawo osafooka kapena kubwelela mbuyo

Artworks motooo kuti buuuuuuuuuu

Tankhala tikukozekela zambiri mu chakachi   zomwe zina mwaizo  sitinakwanitse kuti tikupaseni   koma 2023 tinkhala nanu ...
24/12/2022

Tankhala tikukozekela zambiri mu chakachi zomwe zina mwaizo sitinakwanitse kuti tikupaseni koma 2023 tinkhala nanu tikupasilani zambili
We love you all & we wishing you happy merry Christmas

We are Artworks Malawi happy birthday Lister. We love you 💜Space4Youth  Mindset Youth Club
16/08/2022

We are Artworks Malawi happy birthday Lister. We love you 💜
Space4Youth

Mindset Youth Club

Imeneyi ndi bye bye party ya dolo Daniels Kamchacha MC Chifana Chooloka Buwah Director wa Mindset Youth Club pamene akha...
23/07/2022

Imeneyi ndi bye bye party ya dolo Daniels Kamchacha MC Chifana Chooloka Buwah Director wa Mindset Youth Club pamene akhala aku via ku Kenya. Tiyeni tikaipatse moto. Girls Activist Youth Organisation CISE Malawi Bright Future Youth Club Kayesa Creative Centre, Mchinji Still I Rise 'TINGATHE' Mchinji Drip Geng Twister Gennah Mchinji GFF CSO and Youth Coalition

We attended our Chair's daughter's birthday party. Congratulations Chair Cecilia Nkhuwa for hosting usMindset Youth Club...
18/07/2022

We attended our Chair's daughter's birthday party. Congratulations Chair Cecilia Nkhuwa for hosting us
Mindset Youth Club Bright Future Youth Club CISE Malawi Kapiri Community Development Organization Girls Activist Youth Organisation

Address

McHinji
12345

Telephone

+265999300295

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Artworks Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Artworks Malawi:

Share