28/04/2025
Malangizo kwa ma :artists ,ma producers:ndi ma Director.
Zinthu zozionera kuukulu nzovuta
Ndalama, akazi abwino,fame,udolo.
Ndalama ija imafunika kumaigwirako uli mwana,olo itakhala 20k ,zizingofanana ndi age yakoyo koma at least you got something of value that will give you access to a lot of things your peers won't. When you handle that well zimayenda kutsogoloku.
Akazi abwino:ife tapangako zawana ,sindinakhaleko fisi chiyambireni, I had a choice to say kuti ine Eliza ayi koma ujeniyo. Reason was ndinali Dolo ndipo okometsa zawana plus anzanga oti kwao kunali kochita bwino samatha kucheza ndi atsikana nde ife timadziwa zokonda zawo.
Ukakura nkukhala odziwa zabwino ndi zoyipa, umakhala ndi choice yabwino olo zitakupeza zidebe zopentapenta zija ,you know mkati muli Nyerere umu. Nkadzalemera olo kutchuka ,mkazi wanga ndiyemweyo no matter what. Ndinasankha deal yondikwana.
Mukangotchuka ndikugwira fafanzi basitu mufuna muyesere aliyense mwamupezayo,model kungoshuta naye video basi...phaphapha.
Kamwana kakumpanda kasakupatseni hie ,uyo number mwatenga basi phaphapha!
Mwangolowa chiwewe Fada.
Umunthu ndi kudzilemekeza kumafunika, samalani makobili anu.invest in your career,simudzapedzanso mwayi otakata money muli achichepere choncho.
Female artists,you can do better as well, do not be cheated kuti mudzakhala young and famous mpaka kale,makwinya akukudikirani,mutha fasho time is waiting for you. Kuli ziwanda ndi Matenda ena oposa Aids kunjaku akupha...
Dekhani and manage your income well.
Get one and grow together without serving everyone else. Anthu asamaope dating Celebs....
By Ching'ax●
Osaiwala kutipanga Follow
Acestiga Entertainment