ENI MUDZI

ENI MUDZI Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from ENI MUDZI, Arts and entertainment, Lilongwe.

Congratulations 🎉 Rashley Pamene Nyimbo yake ya LAKWILA yakwanitsa 200k Views in 8days Yomwe Ndi improvement yake yayiku...
01/09/2025

Congratulations 🎉 Rashley Pamene Nyimbo yake ya LAKWILA yakwanitsa 200k Views in 8days Yomwe Ndi improvement yake yayikulu Kwambili 🤝

01/09/2025

Eni Mudzi ayambisa Kale ndewu Kunoo 😂eeeh

This is the Most Booked Artist Right Now Zeze Kingston 👑..
01/09/2025

This is the Most Booked Artist Right Now Zeze Kingston 👑..

31/08/2025

Zeze Afuna apangise Show yaulele Ku Brantley ndipo Azimba Zeze Ndi Jetu ...starting 11AM

Alert MSCE yamalizidwa Kuchongedwa Ndipo Zikunveka Kuti Ma Results Atulutsidwa Friday Likubwelali Nde please Kumayenda M...
31/08/2025

Alert MSCE yamalizidwa Kuchongedwa Ndipo Zikunveka Kuti Ma Results Atulutsidwa Friday Likubwelali Nde please Kumayenda Mutadya Kumeneko ...Maneb will shortly Confirm the date...

Congratulations FADA MOTI Pamene Nyimbo yake Yomwe inamupangisa Kuziwika Ku N'tundu Kwa Malawi Called " Mudyela" yakwani...
31/08/2025

Congratulations FADA MOTI Pamene Nyimbo yake Yomwe inamupangisa Kuziwika Ku N'tundu Kwa Malawi Called " Mudyela" yakwanitsa 1milion Views ......A FADA MWABWELA🤝

31/08/2025

Agogowa nde ABEBA ku TikTok Zuonesa Ayiphula Ndipo Ena akuti angokwatilana Ndi Jetu...

From Inbox Munthu Wina watipeza ati watola Ndalama Ndipo Ngati Pali amene angakwanitse Kunena Amount ya ndalamayi  Ndipo...
31/08/2025

From Inbox Munthu Wina watipeza ati watola Ndalama Ndipo Ngati Pali amene angakwanitse Kunena Amount ya ndalamayi Ndipomwe anataya Akupasa Ndipo akhala akuwelenga Ma Comment....

31/08/2025

Kodi A Rashley Chisangalalo Chokhachokhachi Ichi??? Mpka Zende inuo??

Amidu wadandaula Zomamujambula Akamaipota Nsima kwawo..Izizi sizabwino Gys Kapena aziphikila Ku Chipinda???
31/08/2025

Amidu wadandaula Zomamujambula Akamaipota Nsima kwawo..Izizi sizabwino Gys Kapena aziphikila Ku Chipinda???

31/08/2025

🤧

Ana Amene alemba Mayeso awo A form 4 Chaka chino akufunisisa Kuti Mayeso awo atuluke  Relo Mwachangu Pachifukwa Cha Kusi...
31/08/2025

Ana Amene alemba Mayeso awo A form 4 Chaka chino akufunisisa Kuti Mayeso awo atuluke Relo Mwachangu Pachifukwa Cha Kusitha Kwa syllabus Class yolemba Mayeso Mu form 4 ikhala imene ikulemba MSCE 2026 ..The rest azalemba MSCE mu form 6 Kamba ka Kusitha Kwa syllabus ..Zomwe Zikhale zowawa Kwa Omwe sachita Bwino Nde Ndichifukwa ana ambili akufunisisa Kuti Ma results atuluke Relo...

Address

Lilongwe

Telephone

+265995184222

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when ENI MUDZI posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

//iconSize: [32, 32], //html: '' }) .bindTooltip(name, { //permanent: true, direction: 'bottom', //offset: L.point(12, 25), //opacity: 0.88, interactive: true }) .bindPopup(name); markersLayer.addLayer(marker); } function getMore() { if (gettingMore) { return; } gettingMore = true; var center = map.getCenter(); $.ajax({ url: "/vicinitysearch", data: { lat: center.lat, lng: center.lng, country: "MALAWI" } }) .done(function(data) { var added = 0; data.forEach(function(loc) { if (!locationIds.includes(loc.id)) { var mapLoc = {id:loc.id,lat:loc.latitude,lng:loc.longitude,title:trunc20(loc.name),popupHtml:loc.popupHtml,urlPath:loc.urlPath,pictureUrl:loc.pictureUrl}; locations.push(mapLoc); locationIds.push(loc.id); map._addMarker(mapLoc); added++; } }); }) .always(function() { gettingMore = false; }); } map._clearMarkers = function() { markersLayer.clearLayers(); } }); }, 4000); });