Tinashe studio-prd by anicky

Tinashe studio-prd by anicky Producer anicky, Director j Jollay,balancing by kisanola & kayzo

30/01/2022

Wadzeru saweluza
Koma kuyanjanisa pakalakwika

30/01/2022

1)-Wamantha ------------------ndi ukalamba.
2)------------------sampha utaning'a.
3)-mako-----------sachepa mwendo.

30/01/2022

*Misi* wandimenya mbama atafusa zotenga chakudya?
tamuuza kuti mistake πŸ˜‚πŸ€£πŸ˜‚

*Kodi _mistake_ sikutathauza misi utenge?*πŸ€·πŸΌβ€β™‚οΈπŸ€·πŸΌβ€β™‚οΈπŸ€·πŸΌβ€β™‚οΈ

29/01/2022

Ndikufuna kupita kubanja
munapitako timaseni
Map

28/01/2022

Kodi s jizzy
&
Bee jay
Kiimba
Amaposa mzake ndani?

24/01/2022

Ali nafe ku ma demo
Ndi born kalindo
Aimile manjaπŸ’ͺπŸ’ͺ

24/01/2022

MALAWI amatha
Panyimbo za chikondi
Ndani?πŸ’πŸ’‘

Send a message to learn more

23/01/2022

Kadzi ali ngat mango
Ukamadikila apsye
Ena Amakhala
Akudyera mchele

Call me Anicky

23/01/2022

Kwamene tadzuka bwino
Say thanx to God

18/01/2022

*Nde pali njala Ina imabwera ndi chizungulire, mawu oti mapempheloo ndi kiyi wakumwamba umamva ngati mapemphero ndi tiyi wachinangwa*🀣🀣🀣... Good morning guys tired today ,,,

Yours _famida_

20/11/2021

Address

Malawi Mangochi Id Ya China Jollay
Mangochi
DUNCANNICKSPOETS

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Tinashe studio-prd by anicky posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share