ACE KAY MUSIC

Directions

ACE KAY MUSIC MANGOCHI ARAFURED" ACE KAY MUSIC
(2)

21/06/2026

PA HOME

Madolo🥴🥴
15/06/2026

Madolo🥴🥴

Kmaso Eli Njuchi Pa Mkaz Uyuyu Unapala Sure💔😭
14/06/2026

Kmaso Eli Njuchi Pa Mkaz Uyuyu Unapala Sure💔😭

yes
11/05/2026

yes

Letter to Kineo Madness:Ndiwe Dolo ndiwe Shashaa, umavala bho, umayimba bho, uli ndi sitepe yabho ,uli ndichikondi kwamk...
09/05/2026

Letter to Kineo Madness:

Ndiwe Dolo ndiwe Shashaa, umavala bho, umayimba bho, uli ndi sitepe yabho ,uli ndichikondi kwamkazi.

Mphekesela zikumveka kuti unapanga chibwenzi ndi Mwana wa bigman,nde Mkazi yo ndikumva kuti unamugulira nsapato ndi tizinthu Tina todula.

Koma mwatsoka nkhani ija itatonyoka bigman itamva zoti mfana wawo waguliridwa nsapato ndi Zinthu zina ndi chibwenzi chake Bambo Ake amkazi aja zapezeka kuti zinawanyasa ndipo awotcha zinthu zomwe unamugulira mwana wawoyo.Pepa Pepa

Ukudziwa chani aise ngati nkhani zi zili zowona ukuyenera usamahonge Chikondi Iweyo sunavale nsapato ya 1.5 Mita nde chokamugulira mkazi Ndalama zonsezo chikhale chani, mkazi yo kwawo mkolemela kale Iweyo Ndalama zomwe wawonongazo unakawagayila Makolo ako kuwapatsa ngati Mpamba kuti ayambe business bwenzi utalandila M'dalitso coz 1.5Million ndindalama yambiri.

Koma apa wangoyilowetsa m'madzi ngati msomba next time uzayese kuwapatsa Capital Makolo ako ndipo uzapindula.

Komabe olo nsapato zo aotcha usadandaule Munthu uzikawotcha Show nde nsapato ndikachani,pepa pepa kumayiwonela Mita patali . Langizo la Ulele

tiyeni 🥰
22/04/2026

tiyeni 🥰

Watch, follow, and discover more trending content.

Address

Mangochi

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when ACE KAY MUSIC posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category