Arts Kids Mideya official

Arts Kids Mideya official Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Arts Kids Mideya official, Arts and entertainment, Lilongwe.
(2)

󰟲RTS KIDS MIDEYA󱢏
🎤Maste of ceremonies
🎬Video graphics
🔴Live stream
🎙️Podcast
🖌️T-shirts printing
🖥️Graphic design
󰟬:+265(0)995931134
0883977580
Email: [email protected]
FDH Account: 1400100204365
󰂆Phexy mideya
󰟯 ARTS KIDS MIDEYA OFFICIAL

28/04/2026

Nyimbo za chi Malawi 🇲🇼

11/04/2026

📢 Tithandizeni Kufikira Anthu Ambiri!

Chonde follow page yathu, like, share ndi comment kuti uthenga ufikire anthu ambiri 🙏

Pa post iyi tikuphunzitsa za application ya kuyang’anira ndi kuteteza phone ina yomwe yomwe akugwilitsa ntchito munthu wina:

📱 Kuwona momwe akugwiritsira ntchito phone
🌐 Kuwongolera ma websites omwe amayendera
⏰ Kuyika nthawi yogwiritsa ntchito phone
📍 Kutsata malo omwe ali (location tracking)
🔒 Kuteteza ku zinthu zoipa pa internet

Iyi ndi njira yabwino yothandizira makolo kukhala ndi chitetezo pa ana awo pa digito 👨‍👩‍👧‍👦

👉 Tikufuna kufikira 200 likes pa post iyi kuti tipitilize kuphunzitsa zambiri komanso ma tutorials ena othandiza!

👍 Like
🔁 Share
💬 Comment “DONE” ngati waona post iyi

Zikomo kwambiri chifukwa chothandiza page yathu kukula 🙌

By: Admin Wachichepele

Sponsor by: Arts Kids Mideya official

Ma artwork abho tikupanga tiyakhuleni tikupangileni yanu
11/04/2026

Ma artwork abho tikupanga tiyakhuleni tikupangileni yanu

08/04/2026

Jay Jay Cee Mw kufika ku GENESTLAB FESTIVAL

08/04/2026

Jay Jay Cee Mw live at GENESTLAB FESTIVAL

Azatu tikuwapangilatu
06/04/2026

Azatu tikuwapangilatu

CEO
05/04/2026

CEO

31/03/2026

Ma Design aSmat No👐 Ai

28/03/2026


Ikamati 07:00 pm Tibwela Ndi phuzilo lomwe mungapangile Face Scrub Ya Sugar & Honey kuti Khungu Lanu likhale Lowala!. Pangani follow page yathu komaso share kuti muzilandila zambili

Sponsor by: Arts Kids Mideya official

By : Admin Wachichepele

24/03/2026

Big shout out to my newest top fans! Pemphelo Batala, Voice Lov, Carnex Mw, Don D Kay Mw, Christos Msk Kwajama

Ma Design abho tikupanga
21/03/2026

Ma Design abho tikupanga

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Arts Kids Mideya official posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share