23/06/2026
UP & COMING LILONGWE AREA 23 MAJIGA.
SPECIAL BOY wakozeka kutulutsa nyimbo zake ziwili madzulo ano pa mudzi pano ndi masamba athu onse achedzo.
Special boy ndi oimba yemwe ndi olimbikila Kwambiri komanso ndi oimba yemwe ali ndi nyimbo zambiri.
Uyu wanena kuti music panopa akufuna akhale nayo nkhama. Special boy wapepha anthu pa mudzi pano kuti mumulandile komanso muvele nyimbo zake ndipo mupatse feedback ngati ali oyenela kupitiliza kapena ai chifukwa sakufuna kumaononga nthawi ndikumachita zithu zina zomwe zingamabweletsele ndalama kusiyana ndikumaimba.
Pomaliza special boy wati nthawi ikamati 8:30pm lero nyimbo zake ziwili zikhala zikupezeka pa internet choncho wapepha athu kuti athe kutsitsa ndikuvela nyimbo zo.
komanso ndi nyimbo zomwe zikhale zikupezeka pa internet usikuwu.
Stay tuned.....