Simon Peter

Simon Peter Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Simon Peter, Lilongwe.

Azanga ku South Africa  town muli ziii mukuchita ku opsa kuyenda wekha Have a blessed Sunday đŸ™đŸ»đŸ™đŸ»
21/06/2026

Azanga ku South Africa town muli ziii mukuchita ku opsa kuyenda wekha

Have a blessed Sunday đŸ™đŸ»đŸ™đŸ»

Ife chikoka chathu ndendende ndi Mkulukuta moyo Tipange zimenezi basi..big up Mbuu. Gwamba  chifukwa chondiitana ku Kose...
10/06/2026

Ife chikoka chathu ndendende ndi Mkulukuta moyo

Tipange zimenezi basi..big up Mbuu. Gwamba chifukwa chondiitana ku Kosenti yanu

kwa anthu omwe mukuona ngati sizingatheke aaah bwela muzachitile umboni muzaone mbali ina yaine

Mwaikumbuka nyimbo ija ndinapnga ft Prophet Shepherd Bushiri

Pezani ma tick a konsenti imeneyi muzaone

On this day 10 June 2024 chisoni chachikulu chinakuta dziko la Malawi ...zimkawoneka ngati tikulota ..koma ayi ndithu 1....
10/06/2026

On this day 10 June 2024 chisoni chachikulu chinakuta dziko la Malawi ...zimkawoneka ngati tikulota ..koma ayi ndithu

1. His Honour Dr. Saulos Klaus Chilima
2. Major Flora Selemani Ngwirinji
3. Mr. Lukas Kapheni
4. Mr. Chisomo Chimaneni
5. Ms. Gloria Mtukule
6. Ms.Shanil Dzimbiri
7. Mr. Dan Kanyemba
8. Mr. Abdul Kingstone Lapukeni
9. Colonel Sambalopa.

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Kei Lex, Pilirani Tambala Mw, Prince Mc Neil Imanah, Llyo...
06/06/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Kei Lex, Pilirani Tambala Mw, Prince Mc Neil Imanah, Llyod Funsani, Hestings M Kachere, Elijah Wa Chicco Bandah, Micky Mike, Geoff Mwale, Kingswell Sankhani, Thomas Kamanga, Victor Dweght Matale, Joseph Katambo, Rob Banda, Tyler Braga, Innocent Chiweza MW, Yordan Masunga, Davie Gostino, Andre Alexandre Estevao, Frank Li Tchovan, ÆñdrĂȘĂŠ NĂ„malindih, Gracian H. Saikolo, Dorica Kaipa, Wnstone Kapsera Luwanda, Richmond Off-white, Majiya Junior Davie, Samzy Mkango Mapata, BrĂąstĂŁr KhĂąmĂ»zĂșrĂŠ BÊñdĂŁh, Yang San, Ras Coffee Chirambo, Realsavah Kay Sparta, Robert Moscew Phiri, MC Namukhoyo, Årrdéë ÇzĂ„r, Martha Masimbe Manthalu, Morgan Hazaa N Axel, Lorr Rich, Hassan Phiri, Chris Zimba, Pencildrawing Atist, Thocco Mafiah, Hope L Kalichero, Mude-b Amini, Mlakatuli Peter Masiye, Jozey Jabu, PrĂźĂȘst J ZùßrĂȘ, Kelvin Telfer, Àusçàr K Ndhlovu, Julius Saka, Kinho Lass GS Jr., PĂ€trīçk MĂąsĂŁmbĂ€

Brother in the Lord Judas Iscariot  wayamba Business yoweta timbalame ...let's support our Brother 10500...akumatumiza k...
05/06/2026

Brother in the Lord Judas Iscariot wayamba Business yoweta timbalame ...let's support our Brother
10500...akumatumiza kulikonse komwe mungafune

Simon Peter Kapolo wa Ambuye Yesu......âœđŸ» Kalata yanga yoyamba kupita ku Malawi Government izi zomakhomelera anthu akama...
04/06/2026

Simon Peter Kapolo wa Ambuye Yesu......âœđŸ»

Kalata yanga yoyamba kupita ku Malawi Government izi zomakhomelera anthu akamabwela ndima solution pamavuto omwe aMalawi akukumana nawo zithe

Napoleon Dzombe alindi mtima wofuna kuona dziko la Malawi anthu Ali ndichakudya chokwanila osatiizi zomapangila Dala kuti anthu azifa ndinjala zaukape izi zithe

Munthu mupatseni mapepala omuvomeleza kuti ayambe kupanga Feteleza mudziko mwathu momuno

Inu a Malawi Environmental Protection Authority (MEPA)
Ifetu musatiyese mwanva

Just imagine
factory ilindikuthekela kopanga 40 metric tonnes of fertilizer per hour, komaso tu ati factory yi itha kupanga Feteleza okwanila aMalawi onse kwamasiku 150 .

Kondwani Kachamba Ngwira Mikozi Umatha Daily Makosana Mibawa TV MIJ Online Mafumu Akometsi MBC Digital

Kumakhala bwino ndiwanthu pajaMadolo alero ndimakape amawa komaso Mulungu anatibisila mawa lanthu tiphuzile kulemekeza a...
30/05/2026

Kumakhala bwino ndiwanthu paja
Madolo alero ndimakape amawa komaso Mulungu anatibisila mawa lanthu

tiphuzile kulemekeza aliyense

lero Saturday ndinaganiza zokayendela Amfumu obanda eeee obanda moyo unasitha ...obanda zawo zinayela...

Anthu amasowa zodabwa eti eti eti inu Njoka simuyidziwa Inu mwadya ma tin fish ambiri mbiri ndenkhani ilipati apa Apa ti...
29/05/2026

Anthu amasowa zodabwa eti eti eti inu Njoka simuyidziwa

Inu mwadya ma tin fish ambiri mbiri ndenkhani ilipati apa

Apa tikukaiteleka

Meeting ya azitumiki aMulungu Malumbo Ngaiyaye  wayamba kubela anthu ndalama mudzina la Chakhumi ..nde ndinaganiza zomuy...
28/05/2026

Meeting ya azitumiki aMulungu

Malumbo Ngaiyaye wayamba kubela anthu ndalama mudzina la Chakhumi ..nde ndinaganiza zomuyendela kuti timuuze kuti asiyiletu mchitidwe wakusaweluzika wu.

Koma Malomwake ndaona kuti naneso ndiyambe kulandila Chakhumi molowa m'manja

Ndalama alinazo koma Swagger sangamake

Zeze pamodzi ndi ine  Simon Peter tikuti Happy Birthday to  The Kingstons MW Doro - Simon - Zeze Uyu ndi Age met wathu ....
26/05/2026

Zeze pamodzi ndi ine Simon Peter tikuti Happy Birthday to The Kingstons MW Doro - Simon - Zeze

Uyu ndi Age met wathu ... Simon Peter 52 yrs. ZeZe 45 yrs Our Queen 👑 Dorothy 32 yrs

Wa Mkulu ndiMulungu anthu timangosiyana tsiku komaso chaka chobadwila ena amabadwa changu onena mochedwelapo

Uyu amapeleka molowa mmanja ku Church kwanthu

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Simon Peter posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share