Tisinthe

Tisinthe Tisinthe! Produced by Theatre for a Change, Malawi.

is Malawi's only live interactive radio drama show which gets us involved and talking more openly and honestly about Sexual reproductive health and rights.

Kukhala ndi mwana wakhungu la chi albino ndiyekuti mayi sanayende bwino. Kodi izi ndizoona kapena zabodza?Tipatseni maga...
14/07/2026

Kukhala ndi mwana wakhungu la chi albino ndiyekuti mayi sanayende bwino. Kodi izi ndizoona kapena zabodza?

Tipatseni maganizo anu ndipo ife tiwerenga mu program ya Tisinthe lero Lachiwiri pa 14 July 2025 @ 2:00 PM to 3:00 PM

ENGLISH
Having a child with albinism is the woman’s fault and means she had a sexual relationship with a white man. Is this true or false?

Give us your views and we will read them out during our Tisinthe live radio program Today Tuesday 14 July @ 2:00 PM to 3:00 PM live on Zodiak

Kodi pakati pa achibale ndi anthu adera, akumachitira chipongwe anthu akhungu la chi Albino mochulukira ndi ndani?Tipats...
07/07/2026

Kodi pakati pa achibale ndi anthu adera, akumachitira chipongwe anthu akhungu la chi Albino mochulukira ndi ndani?

Tipatseni maganizo anu ndipo ife tiwerenga mu program ya Tisinthe lero Lachiwiri pa 07 July 2025 @ 2:00 PM to 3:00 PM

ENGLISH
Between family members and community members, who is increasingly mistreating people with albinism?

Give us your views and we will read them out during our Tisinthe live radio program Today Tuesday 7 July @ 2:00 PM to 3:00 PM live on Zodiak

Kodi ulipo msika wa mafupa/ziwalo za munthu wakhungu la chi Albino?Tipatseni maganizo anu ndipo ife tiwerenga mu program...
30/06/2026

Kodi ulipo msika wa mafupa/ziwalo za munthu wakhungu la chi Albino?

Tipatseni maganizo anu ndipo ife tiwerenga mu program ya Tisinthe lero Lachiwiri pa 30 June 2025 @ 2:00 PM to 3:00 PM

ENGLISH
Does a market exist for the bones and body parts of people with albinism?

Give us your views and we will read them out during our Tisinthe live radio program Today Tuesday 30 June @ 2:00 PM to 3:00 PM live on Zodiak.

28/06/2026

Big shout out to my newest top fans! Gift Jonathan Banda, Chakudza Alekadala Elias, Benard Chimtengo, Josaya Josaya, Acyatu Mwamadi Moyo, Dainner Chimpambo, Sheila Makwinja, Emily Nyerere

Kodi ndi udindo wandani kumuteteza munthu  wa khungu la chi Albino?Tipatseni maganizo anu ndipo ife tiwerenga mu program...
23/06/2026

Kodi ndi udindo wandani kumuteteza munthu wa khungu la chi Albino?

Tipatseni maganizo anu ndipo ife tiwerenga mu program yathu ya Tisinthe lero la Chiwiri pa 23 June 2026 pa Zodiak.

ENGLISH
Whose responsibility is it to protect a person with albinism?

Give us your views, and we will read them out during our Tisinthe live radio broadcast today, Tuesday, 23 June @ 2:00 PM - 3:00 PM.

Munthu wa khungu la chi albino samamwalira amangosowa. Kodi izi ndizoona kapena zabodza?Tipatseni maganizo anu ndipo ife...
16/06/2026

Munthu wa khungu la chi albino samamwalira amangosowa. Kodi izi ndizoona kapena zabodza?

Tipatseni maganizo anu ndipo ife tiwerenga mu pologalamu yathu ya Tisinthe lero lachinayi pa 16 June 2026 @ 2: 00 - 3:00 PM masana.

ENGLISH
People with albinism do not die; they simply disappear. Is this true or false?
Give us your views, and we will read them out during our Tisinthe live radio broadcast today, Tuesday, 16 June @ 2:00 - 3:00 PM.

Kodi munthu wa khungu la chi albino ali ndi kuthekera ngati munthu wina aliyense?Tipatseni maganizo anu ndipo ife tiwere...
11/06/2026

Kodi munthu wa khungu la chi albino ali ndi kuthekera ngati munthu wina aliyense?

Tipatseni maganizo anu ndipo ife tiwerenga mu pologalamu yathu ya Tisinthe lero lachinayi pa 11 June 2026 @ 3:00 - 4:00 PM masana.

ENGLISH
Do persons with albinism have the ability just like any other person?

Give us your views, and we will read them out during our Tisinthe live radio broadcast today, Thursday 11 June @ 3:00 - 4:00 PM.

Kodi kusintha malamulo kuti azilora amayi ndi atsikana kuchotsa mimba munjira yoyenera kungathandize kuchepetsa imfa ndi...
09/06/2026

Kodi kusintha malamulo kuti azilora amayi ndi atsikana kuchotsa mimba munjira yoyenera kungathandize kuchepetsa imfa ndi mavuto odza Kamba ka uchemebere?

Tipatseni maganizo anu ndipo ife tiwerenga mu pologalamu yathu ya Tisinthe lero lachinayi pa 9 June 2026 @ 2:05 masana pa Zodiak.

ENGLISH
Can the legalization of safe abortion help reduce maternal deaths and related complications in Malawi?

Share your views with us, and we will read them out during our Tisinthe live radio program today, Tuesday, 9th June 2026, at 2:05 pm on Zodiak Radio.

07/06/2026

With Tisinthe – I just made it onto their weekly engagement list by being one of their top engagers!

Malamulo oletsa kuchotsa mimba ndi omwe akukakamiza amayi ndi atsikana, kuchotsa mimba munjira zosayenera. Kodi izi ndiz...
04/06/2026

Malamulo oletsa kuchotsa mimba ndi omwe akukakamiza amayi ndi atsikana, kuchotsa mimba munjira zosayenera. Kodi izi ndizoona kapena zabodza?

Tipatseni maganizo anu ndipo ife tiwerenga mu program ya Tisinthe lero Lachinayi pa 4 June 3:05 - 4:00 Masana pa Zodiak

ENGLISH
Malawi's restrictive abortion laws are forcing women and girls into unsafw abortions. True or false?

Give us your views, and we will read them out during our Tisinthe live interactive radio program today, Thursday 4 June 2026 at 3;5 to 4:00 pm.

Address

Off Likuni Road
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Tisinthe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Tisinthe:

Shortcuts

Share

Category