08/04/2026
Izi ndi zomwe The Jack show wafotokoza zokhudzana ndi nkhondo Ya Iran ndi Israel
Perspective
- Nkhondo isanayambe, Strait of Hormuz inali yotsegula ndipo aliyense amadutsa ulere. Pano, adzipanga charge fee pafupifupi 2million. Pamadutsa ma ship ambiri pa tsiku. Iran ndi Oman ilemela.
- Panali chiyembekezo chakuti mayiko ena aphula mafuta nkulemera, koma abwerako chabe.
- US yaluza ma military base 11 ku ma gulf states komaso ma radar system. Patenga nthawi kuti izi zimangidwenso...ngati zitamangidwenso.
- Panali chiyembekezo chakuti kuphedwa kwa Ayatollah kupangitsa dziko la Iran kuti libalalike ndikulowetsa anthu akunja, koma zinayenda mwa opposite, anthu anayanjana against anthu akunja.
- Mayiko amene anakana kulowelera ndi kuthandiza US, anayibalalitsa...UK, Italy, Spain, Japan, South Korea, Australia, France ndi ena
- Before nkhondo, Iran inali under ma sanctions oyipondeleza. Pano akufuna ma sanctions achotsedwe.
Kalelo
Ku DRC, anapha Lumumba, dziko linabalalika.
Ku Venezuela, anagwira Maduro, dziko linagwada
Ku Libya, anapha Gaddaffi, dziko linafoila
Nazo mzika zochuluka za ku US zinadana nayo nkhondoyi.
Ndikukayika ngati itayambilenso... onse atuluka ndi kamfuno.
A Ku Iran 2000 aphedwa. Enawo ma numbers enieni akudziwa okha.