Pa Bwalo Malawi

Pa Bwalo Malawi Home of latest News and Entertainment

14/08/2026

Landlord Apa kupuma ntchito wagwira kale 🫑

Amene anali wamkulu wa Malawi Broadcasting Corporation(MBC)Brian Banda watisiya Mmawa wa lero kuchipatala cha mwai wathu...
08/08/2026

Amene anali wamkulu wa Malawi Broadcasting Corporation(MBC)Brian Banda watisiya Mmawa wa lero kuchipatala cha mwai wathu πŸ’”πŸ’”

Mzimu wa brian Banda uwuse mtendereπŸ•ŠπŸ•ŠπŸ’”πŸ˜­

Uku ndiye timati kuwasutsula ma well wishers pachilonda..Spanner yemwe amadziwika ndi kudya walemba izi ku page kwake ch...
30/07/2026

Uku ndiye timati kuwasutsula ma well wishers pachilonda..Spanner yemwe amadziwika ndi kudya walemba izi ku page kwake chonsecho mene amapita ku ulendo wake opita ku Nigeria anali daily kupempha chithandizo kwa ma well wishers kuti amuthandize kugula ticket ya ndege kupita ku nigeria ena omwe anamuthandiza ndi omwe akuwanyoza kuti ali busy kuyendetsa ma wheelbarrow ku Jubeki
Kodi Ameneyu Spanner yy akazabweranso kuti akufuna akwereso ndege Muzamusokhera? Ndimene akuyankhuliramu

30/07/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Differentguy Manda, Akimu Pazani, Khoo Mw, Real Goats

27/07/2026

Kucheza Kwa Bwanji Uku Man Chippie🀣🀣

πŸ’”πŸ˜­πŸ˜­
25/07/2026

πŸ’”πŸ˜­πŸ˜­

Ka dziko kang'onong'ono koma Zochitika phwilikiti My Malawi WhyπŸ’”πŸ’”πŸ˜­πŸ˜­Nanga mpaka Admarc kuoletsa Chimanga Chokwana 70 Metr...
24/07/2026

Ka dziko kang'onong'ono koma Zochitika phwilikiti My Malawi WhyπŸ’”πŸ’”πŸ˜­πŸ˜­Nanga mpaka Admarc kuoletsa Chimanga Chokwana 70 Metric Tonnes

Good Morning..Mwadzuka Bwanji..Mawa Wawemi..Mwauka Bwanji..Mwayuka Uli....Mawa Abwino..Mawa Gahala..🌝🌝🌝🌝🌞
24/07/2026

Good Morning..
Mwadzuka Bwanji..
Mawa Wawemi..
Mwauka Bwanji..
Mwayuka Uli....
Mawa Abwino..
Mawa Gahala..
🌝🌝🌝🌝🌞

Mtsogoleri Wa FAM Fleetwood Haiya Wapereka Jersey ya Scorchers Ngati Mphatso kwa Mtsogoleri wa FIFA Gianno Infantino kom...
23/07/2026

Mtsogoleri Wa FAM Fleetwood Haiya Wapereka Jersey ya Scorchers Ngati Mphatso kwa Mtsogoleri wa FIFA Gianno Infantino komanso kwa ena omwe anali Akatswiri ampira wamiyendo

Team yathu ya Scorcher yomwe ndiya azimayi ikhala ikusewera nawo WAFCON izi Zikutathauza kuti team yathu ya scorchers yazigulira Mmalo ku FIFA kuposa azibambo athu the FLAMES omwe zitha kukhala zochititsa manyazi kukapereka Jersey yawo pomwe olo ku Afcon Zimawavuta kupitako

Kuyankhula kwa Bwanji uku 🀣🀣🀣
23/07/2026

Kuyankhula kwa Bwanji uku 🀣🀣🀣

Address

Lilongwe

Telephone

+265888493355

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pa Bwalo Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share