Akometsi

Akometsi We promote brands, entertain people and exaggerate issues. No sad moments here.
(215)

HAPPY BIRTHDAY TO Jae Cash’S MOTHER! ❤️🎂Zambian rap heavyweight Jae Cash is today celebrating a very special woman in hi...
26/08/2026

HAPPY BIRTHDAY TO Jae Cash’S MOTHER! ❤️🎂

Zambian rap heavyweight Jae Cash is today celebrating a very special woman in his life his beloved mother, as she adds another year to her life.

The rapper has taken time to appreciate and honour the woman who gave him life and has been part of his journey.

Happy Birthday, Mama Jae Cash! 🎂🥂

Admin Wa Zambia.

26/08/2026

Ndi ma level avutawa

Timuwoneretu asanatchukeUyu ndi Arnold Tengani, dzina loyimbira Kamanat Steez, m’modzi mwa anthu amene apanga register k...
26/08/2026

Timuwoneretu asanatchuke

Uyu ndi Arnold Tengani, dzina loyimbira Kamanat Steez, m’modzi mwa anthu amene apanga register kuti apange nawo za Fan-Rated, program ya Akometsi yomwe ikhale ikupanga promote ma upcoming artists.

Kamanat Steez amayimba Afro ndipo kunenetsa kuti afika kuma finals sakuwopa aliyese poti inu ma fans mumukonda pomupatsa mavote okwanira kuti afike kuma finals.

Walonjezanso kuti akadzatchuka adzakhala wa khalidwe labwino losakonda akazi. Kodi ameneyu akuwonekerani bwanji? Atisunga? Nafenso tikudikira kuti timuwone. Tiyeni timulangize uku tikumulandira.

If you haven’t registered for Fan-Rated, make sure to do so as space is limited and given to those who come first.

Nde kuli zi ana izi zama style a bass, china chaku Afro, china chaku Trap 🔥🙌🏾
26/08/2026

Nde kuli zi ana izi zama style a bass, china chaku Afro, china chaku Trap 🔥🙌🏾

26/08/2026

Mumgomenyedwapo za ziiii. Lembani comment mukufunayo muone

Congratulations to Fedson Mtetha on graduating today from UNIMA with a Bachelor of Science in Family and Consumer Scienc...
26/08/2026

Congratulations to Fedson Mtetha on graduating today from UNIMA with a Bachelor of Science in Family and Consumer Sciences 🎉

26/08/2026

Kungokweza mkono pa family meeting, aliyese amvekere zopempha zikhala pamapeto
🔨

26/08/2026

Ndi zimene zikuchitika week imeneyi, be judged accordingly

Akuchita kukhalana ngati 'save the date' 👏🏾
26/08/2026

Akuchita kukhalana ngati 'save the date' 👏🏾

Happy birthday Toptik
26/08/2026

Happy birthday Toptik

Address

HewKam Office Complex, Area 43 (Opposite Planet Events)
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Akometsi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Akometsi:

Shortcuts

Share