Pabwalo360MW

Pabwalo360MW Kwacha tive zithu Pabwalo📌🇲🇼

your trusted source of news and entertainment🔥✔️

Bomba latimkenao lapha Anthu 31 ndikuvulaza anthu pafupifupi 170 ,zachitika pamalo opephelela a silamu pa mzikiti otched...
06/02/2026

Bomba latimkenao lapha Anthu 31 ndikuvulaza anthu pafupifupi 170 ,zachitika pamalo opephelela a silamu pa mzikiti otchedwa Shia Muslim mudziko la Pakistan muzinda wa islamabad

Team ya Ekhaya FC yatulusa chikalata chomwe chi kusonyeza Kuti ubale omwe unalipo pakati pa team ndi designer oziwika bw...
06/02/2026

Team ya Ekhaya FC yatulusa chikalata chomwe chi kusonyeza Kuti ubale omwe unalipo pakati pa team ndi designer oziwika bwino otchedwa wathesedwa sopano posatila posagwirizana ndimomwe Royview amayendesela zithu zake

Phindi zingapo zapitazi gulu lina lazigawenga za mfuti lagwila a Sammer sacraine omwe ndimkulu wa hotel 🏨 yoziwika bwino...
06/02/2026

Phindi zingapo zapitazi gulu lina lazigawenga za mfuti lagwila a Sammer sacraine omwe ndimkulu wa hotel 🏨 yoziwika bwino ya Crossroads mu mzinda wa Lilongwe

Zigawengazi zawagwila akusika galimoto pa hotel pompo ,Ndipo zinakwanisa kuwakakamiza kulowa mgalimotomo kenako zinawombela mwamba kawiri ndimfuti

Neneli wa a police wa Lilongwe wasimikiza za nkhaniyi

Tikupasilani zambiri

‘’Misonkho kulikose amalawi tithawila Kuti’’?. ili ndifunso lomwe amalawi akufusana munyengo yamisokhoyi ,nanga ndiku be...
05/02/2026

‘’Misonkho kulikose amalawi tithawila Kuti’’?. ili ndifunso lomwe amalawi akufusana munyengo yamisokhoyi ,nanga ndiku bet komwe

Ai pepa Malawi wanga 🇲🇼💔🙌

Pomwe madela ambiri mudziko lamalawi akudandaula nding’amba yomwe yaumisa mbewu zakumunda ma report akuwonesa Kuti madel...
05/02/2026

Pomwe madela ambiri mudziko lamalawi akudandaula nding’amba yomwe yaumisa mbewu zakumunda ma report akuwonesa Kuti madela ena akumwela ndi pakati padziko lamalawi monga Blantyre ,Dedza ndi madela ena ozungulira mvula ilimkati kugwa lero patha masiku angapo osagwa

Mu report likubwelali admin wathu alowa live kutiwonesa momwe ikugwela


Address

Lilongwe

Telephone

+265889758166

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pabwalo360MW posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Pabwalo360MW:

Share