Kondwani Alufaneti

Kondwani Alufaneti Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Kondwani Alufaneti, Poet, Lilongwe.
(1)

25/06/2026

Sindikusintha maganizo obwera December, apa tabwera ku trip any time I will go back.

24/06/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Laurent D Msonthi, Soza Ndaferankhande, Nyong'o Mwandire, Gregory Banda, David Mwasalapa, Skga Abner K-arts, κΉ€λ„ν˜„, Wait Pangorine, Ayuba Saleh, Kijana Mxtaarab

24/06/2026

Zoti chikondi ndi anthu awiri wa chitatu ndi osokoneza Zina ndi zaboza pano Oro awiri nokhanokha mumasokonezana πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ₯±πŸ™Œ

23/06/2026

Ngati simukufuna ingonenani nanga faifi handede mwana wa eni akaitenga kuti β“πŸ€£πŸ€£

22/06/2026

kunena chilungamo mene kukuziziliramu chikuopsa ndi CHIBAYO

20/06/2026

zoti mwapanga gala ya form 4 taona ma results muzationeseso 🀣🀣🀣

19/06/2026

BWABWALI CDSS ndi sukulu yomwe ili Boma la Chikwawa ndipo ndi imene ndidasankhidwira. Ndikumeneso ndidayamba kulemba ndakatulo chifukwa cha support yochuluka. Mpaka pano ndakatulo zikadakomabe pa BWABWALI CDSSοΏ½

19/06/2026

Ngati wafika form 4 ndi graduate ameneyo kumampasa ulemu

18/06/2026

Inde za padziko ndizotsala koma zikamazatsala zizaziwanso kuti sife anthu amasewera πŸ€£πŸ€£πŸ€£πŸ™Œ

mboni mungaikhulupilire ❓ πŸ€£πŸ€£πŸ€£πŸ™ŒπŸ™Œ
16/06/2026

mboni mungaikhulupilire ❓ πŸ€£πŸ€£πŸ€£πŸ™ŒπŸ™Œ

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kondwani Alufaneti posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category