19/02/2026
bambo wina watchetcha Chimanga atawapeza ankazi awo akupanga zadama ndi mamuna yemwe anasiyana naye ,abambo anyuwaniwo anagulitsa njinga yawo kugula feteleza woti amayi wo athire munda komanso amasamala ana awiri a bambo wakaleyo,popsa mtima wachotsa chonse chimanga ,ena akuti anakadikilira nthawi yokolora kuzachitenga chose ,ena akuti wachita bwino π€£ imu mukuti bwanji??