Kaphatiye Primary School

Kaphatiye Primary School Know How The School Is Perfoming And Some News Surounding The School

15/07/2022

Have a fantastic holiday ana std 8 waiting patiently for anew levelβ€β€β€πŸ‘πŸ‘πŸ‘πŸ‘πŸ‘πŸ‘πŸ‘πŸ‘πŸ‘

12/07/2022

Congratulations ana nose pamene mukuyamba mayeso odzigulira Malo kukayamba moyo wa Ku secondary.much❀❀❀

12/10/2020

1st dae of school.
_ no uniform;no learning
_no mask_no learning
_std1&2 ; monday and thursday
_std3&4;tuesday & friday

19/09/2020

School ana astd 8 anatsakulira kungophuzrak 1wk akt district mock.. Soon ayamba mayeso awo aboma.

Ana ali ndi umwayi oti atha kuchita bwino mayeso akubwelawa??

Ana ambiri andiuza kuti akangolakwa mayeso amenewa,sazabweleraso mkalasi...

NOTE: Pa 12october std1 up to std7 akusegulira school. Alimbikiseni ana anu kuti akayambe sukulu.

16/08/2020

President D.R Lazarus chakwela has announced the opening of schools in early september. what is your comment?

13/08/2020

Ndinakumana ndi ana oposa 10. Anena zoti sukulu ikayamba ali ndi nkhawa coz mabuku anataya anasowaso sakuziwa kuti atani

16/04/2020

Please ana inu mabuku osataya, tamawelengani any time u'll be told to go back to school. Its your chance to cover alot.

04/04/2020

How is holiday?

Are you reading? mainly you learners.

Dont just stayn its your chance to cover alot.

02/04/2020


Malawi has registerd three cases of

confirmed this.

30/03/2020

NOTE:
As we are on this holiday,

Please you are not allowed to play in the classrooms, once found u'll pay 20pin.

22/03/2020

School ana akutsekela mawa monday 23/03/2020

Malingana ndi kulankhula kwa peter mutharika kuti ma sukulu ose atsekedwe

01/03/2020

Mbava zaba mmanyumba amaziphuzitsi dzana.

Fuso ndikumati ntchito yolonda ndi chani mpaka kuba makomo 4?

Address

Ntchisi
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kaphatiye Primary School posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share