Chisapo likuni Chigwili - CLIC Awards

Chisapo likuni Chigwili - CLIC Awards Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Chisapo likuni Chigwili - CLIC Awards, Arts and entertainment, Area 56, Lilongwe.

12/03/2026

Abale tatchulani maina ama HD studios aja mwina titumizeko oimba ena a mmudzimu fukwatu ma pikitchala akumagwiritsa pama artwork ngati ajambulira wayilesi. 🙌

Tatchulani tidziwe nawo

Wakhala koyambirirayu ndi gospel artist. Wachiwiriyo amaimba nyimbo za mowa komanso tsiku silimatha osakhalako sober (ka...
12/03/2026

Wakhala koyambirirayu ndi gospel artist. Wachiwiriyo amaimba nyimbo za mowa komanso tsiku silimatha osakhalako sober (kamowa) winayo nde Kaya amatani koma amaimbanso chabe amakhala Kwa msanga.

Oimba wa gospel yu, wamowayu, wakwasanga yu anatulutsa nyimbo yachikondi pa valentine's Day komano panopa ayamba kulimbirana umwimi wa nyimboyo 🙌 aliyense akungoti ndi yake ATI chifukwa anthu ayamba kuikonda.

Mwina muzionera ngati simunaoneke kenako mutiuze kuti mwini wake wamyimboyo ndindan 🙌

Tiuzeni

Pena pake oimba akulu akulu akwathu kuno Ku chinsapo Likuni chigwiri akukakamiza kuimba. Remember back days D-all Ulendo...
22/02/2026

Pena pake oimba akulu akulu akwathu kuno Ku chinsapo Likuni chigwiri akukakamiza kuimba.

Remember back days D-all Ulendo anaimba nyimbo ndi Martse anangomveka kanthawi komweko. Kenako kunali ziii. Koma amaimbabe koma nyimbo zake zopanda mitu kweni kweni. Padutsa zaka zambiri tsopano APA ndipomwe akadzimatilira Kwa Rashley Mw aimba nayenso nyimbo kuyesetsa kuti mwina abwerere mu game komatu ai tivomereze ndi nthawi ya achina chixy komanso a china matrix.

Anyways mwina taimvereni ndinuo nyimboyo🙌🙌🙌🙌

artist of the week Picial Artist
22/02/2026

artist of the week
Picial Artist

 kar sir Blanka watulutsa kanema watsopano yemwe akumutcha dzina lakuni gheto yanga . munyimboyi wapanga feature ankake ...
03/02/2026

kar sir Blanka watulutsa kanema watsopano yemwe akumutcha dzina lakuni gheto yanga . munyimboyi wapanga feature ankake ammunition mwawo komaso ku 36 ku ma shop 8 main awo ndi monga sir spark x sir bar lakanta x yush land x worl icaan x moxy

Enjoy the videos and music you love, upload original content, and share it all with friends, family, and the world on YouTube.

27/12/2025

tikuonatu,
Tien tikumane chaka cha mawa

Kulinso nkulu uyu.Andie Mw, Dolo wa kwachinsapo.Gospel artist, show organizer, mwini wake wa anthu ntomwefe brand.Inu mu...
18/07/2025

Kulinso nkulu uyu.
Andie Mw, Dolo wa kwachinsapo.
Gospel artist, show organizer, mwini wake wa anthu ntomwefe brand.

Inu mumamudziwa ndi ziti?

komanso mkulu uyu amatha kuimba. mwamudziwa? tamutchuleni dzina tione ngat mwamudziwa
12/06/2025

komanso mkulu uyu amatha kuimba. mwamudziwa? tamutchuleni dzina tione ngat mwamudziwa

12/06/2025

This year it's gonna be fire chifukwa tikupereka mwayi kwa aliyense amene Ali ndi ma project kuti timupangile promote .

11/06/2025

Mwina mutithandize ndinu, Malo abwino opangira show angakhale ati?

Kopanda chipwilikititu 😂

27/01/2025

Mwina ena simudziwa, mwachinsapo muli ma website awiri omwe mukhoza kupanga upload nyimbo zanu. Ghetto ndi self container
1. Just Malawi .com
2. anthu ntomwefe .com

Address

Area 56
Lilongwe

Telephone

+265882432303

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chisapo likuni Chigwili - CLIC Awards posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share