Chinsapo arts theatre

Chinsapo arts theatre We are a dynamic Malawian youth group revolutionizing community development through arts.

Established in 2016 as Mzathu Youth Club, we address pressing issues like environmental management, social welfare, youth development and agriculture.

tati tithokeze kamba ka support yomwe munatipatsa pa mwambo wathu omwe tinali nawo dzulo (14 MAY 2026) wa ukwati ongoyes...
15/05/2026

tati tithokeze kamba ka support yomwe munatipatsa pa mwambo wathu omwe tinali nawo dzulo (14 MAY 2026) wa ukwati ongoyeselera ( MOCK WEDDING). Cholinga cha ukwati chinali kupeza ndalama zomwe tikufuna kuthandizila mbali zina za bungwe lanthu la Chinsapo Dancers Association lomwe cholinga chake mkufuna kutukula luso lamavinidwe.

mongobwereza ukwati unali oyeselera ndipo akwati athu jonathan komanso ireen sibanja munjila ina iliyonse. iwowa ndi amodzi mwa anyamata ovina, jona kuchoka ku Beginners Dancing Crew ndipo ireen kuchoka ku Chinsapo arts theatre

zikomo chifukwa chotimvetsetsa komanso chikondi chanu🙏

14/05/2026
Ife timafila chinsapo arts theatre!! Nanga iweeee??? Big shout out to my newest top fans! Travi Lion, Hanafi Yusufu, Itz...
13/05/2026

Ife timafila chinsapo arts theatre!! Nanga iweeee???

Big shout out to my newest top fans! Travi Lion, Hanafi Yusufu, Itz Migirl, Nårçø Dyadya, Miove Kanola, Mtende L M***a, Madalitso Chengula, Rashid H Lion, Hàŕriçè Chîùşîwä, Bless J Basikolo, Blandina Mwale

mmawatu ili... tiyeni pa water users tikasangalale ndi mock wedding... its begginers dancing crew Vs Chinsapo arts theat...
13/05/2026

mmawatu ili... tiyeni pa water users tikasangalale ndi mock wedding...
its begginers dancing crew Vs Chinsapo arts theatre

dont forget MK1000 Pakhomo...
zonsezi ndi Chinsapo Dancers Association

see you there!!!

its another cakes day.. happy birthday madam Ireen Chembezi lero muli pa bill yathu inuyo...enjoy your day
13/05/2026

its another cakes day.. happy birthday madam Ireen Chembezi lero muli pa bill yathu inuyo...
enjoy your day

one simple man with great talent...happy birthday mr Director of dancing, mumatiyika pa map ndi ma set anu anyatwaenjoy ...
12/05/2026

one simple man with great talent...
happy birthday mr Director of dancing, mumatiyika pa map ndi ma set anu anyatwa
enjoy your day bwana 🫶

08/05/2026

It was an honor to spice up this event that was organized by member of parliament for kamphuno constituency Hon Khadija Leah Chunga . The event was championed to end child marriages through protecting the dignity and future of a girl child and also promote Elect Her and Retain her campaign. Present on the event was the Second deputy Speaker of malawi parliament, Honourable Esther Jolobala and other female members of parliament from across SADC region.

Down here is our full performance during the event

Chinsapo arts theatre


Address

Kakule Primary School
Lilongwe

Telephone

+265883272561

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chinsapo arts theatre posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Chinsapo arts theatre:

Share

Category