WISCky DY POET

WISCky DY POET Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from WISCky DY POET, Poet, Lilongwe.

08/08/2023
07/08/2023

Push other's first then you pushed by support

06/08/2023

Ma ingredients ya OKONDEDWA wanga

Unali usiku wakusadziwa
Pomwe chisuphi anandigoneka
Lofanalo tulo,nandithola yakumazele
Nthiti
Napangala wina wa mawonekedwe
Okongolo woti azindifunditsa kunja
Kukazizila

Sikuti chinali chonkhancho chomwe anapangila
okondedwayu
Koma muja apangira chokoleti kumixer mixer
Zinthu
Ndimomwenso anpangila wotchecwa m'kaziyo
Kuwumba khope yake anayikakukongola komwe
Kumawonekera m'maso mwake
Komaso chimwemwe chomwe masaya ake
Amalengeza
Wopangayo anazindikila kuti sipakukwanila
Moti sanachitire mwina koma kuyika akasupe
A unchi m'milomo mwake

Sanasiilenso pompo koma mkamwa mwake
Nayikamo chitsime chamkaka ndincho lilime
Lodzaza nditinyimbo tachikondi
Atafika pamenepo anayima kaye, namuyang'anitsitsa
nadzifusa nchiyani chitsara
Kenako anakutira mutu wake ndi nduwila
Ya tsitsi la zindo
Uku ndiye kunali kumalinza kukonza kukonza
Yake yokongola nkhope yonkhala ndi
Timaso tangati takhunda

Koma tchito yotamandikayitu sikuti. Inangothela pomwepo............(ikupitililabe..pangani like this page kuti munve zambili
Kuphatikinzapo mavidio komaso audios

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when WISCky DY POET posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category