02/03/2026
Iran posachedewapa about 5 minutes ago yatumiza zimabomba kuposa zimene inatumiza mamawa . Iyo yapereka dzina kuti " Pita ku Malo a adani " Iran yati dikilani zigwe zikafika muone mphamvu yake. Sizikuziwika kuti akuzipitisa kuti . Tiziwane zikagwa
Source: Kondwani Kachamba Ngwira.