Ella Cossam

Ella Cossam poetry

09/02/2026

Yabweranso valentine tikhumbire 😂

Pomwe mukudikira kuti muzandibooke inuyo mukazapeza nthiti mukhonza kubandichita recommend kwa achibale ndi anzanu.Mulun...
23/12/2025

Pomwe mukudikira kuti muzandibooke inuyo mukazapeza nthiti mukhonza kubandichita recommend kwa achibale ndi anzanu.

Mulungu akudalitseni pamene mukuchita chokomachi

Zikomo

Kodi simukukwatira bwanji?? Tandichiteni book ndipeze ya mchere kaa😂😂
18/07/2025

Kodi simukukwatira bwanji?? Tandichiteni book ndipeze ya mchere kaa😂😂

Mukutani??Kaoneleni sulingana Ku YouTube mwina mupeze Ka motivation kogwa muchikondi😂
26/04/2025

Mukutani??

Kaoneleni sulingana Ku YouTube mwina mupeze Ka motivation kogwa muchikondi😂

Sulingana written and cited in Malawis vernacular (Chichewa) is a poem that appreciates love. A lady praises his man for being so unique in so many different...

As an MC am all set to spice up your events in this 2025Kindly book me on 0998068999Zikhoswe, maukwati, bridal shower ko...
17/01/2025

As an MC am all set to spice up your events in this 2025
Kindly book me on 0998068999
Zikhoswe, maukwati, bridal shower komanso zochitika zosiyanasiyana ndiyankhuleni kamtengo pang'ono

14/11/2024

Kwacha titulutse ndakatulo 🤝😅

1:30 pm ngoo!

Mawa (LACHINAYI pa 14 Nov) ndikakhala MULENDO PA WAYILESI ya times nthawi ya HAFU 1 MASANA kukaiphwetula mpakete ndakatu...
13/11/2024

Mawa (LACHINAYI pa 14 Nov) ndikakhala MULENDO PA WAYILESI ya times nthawi ya HAFU 1 MASANA kukaiphwetula mpakete ndakatulo ya vuto ndi inu chonde tiyeni tizakhalire limodzi.

Kodi inu mukuona ngati ndakatulo yatsopanoyi yanyamula uthenga wanji?

The best guess wins Ka 5 pin
Winner will be announced after the premier mawa 2 koloko masana

Address

Lilongwe

Telephone

+256700356678

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ella Cossam posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Ella Cossam:

Share