14/04/2024
Azitsogoleri lero tinakwera minbus ulendo wakwa manje ukuu🚌
Kenako pa stage penapake panazakwela amayi ndi mwana wao,komatu mwanayo anali owala💎 nde munali nyashii yopalamulisana🤤.
Her age ranges from 16-19 years 😎
Koma mwatsoka ndi malo amapitawo ndalama yawoyo simakwana anthu awili nde conducter suggested kuti aikane pamwendo, 🙄💔
Atsogoleri umunthu waine sumalola kuti amai achikalambilewo aike mwana mkulukulu pamwendo🙅 nde I volunteered kuti akhale pamwendo panga😁🕴️
Pamene mayiwo amati azivomela offer yanga bambo ena ooneka anyonga🏋️ anazazipeleka kuti akhala pamwendo pawo nde mayi wo kukhala ngt sadziwa chikomekome ndi cha nkhuyu🤦 avekele.
"Tathokoza malume pofuna kuthandiza koma ndekut angokhala pamwendo pa awowo inuo tisakuvuteni kwambili🙏"
Ine shaa💔 I really wanted to do good deed nde ndinayesa kuwamasula kuti asaone nyama yangayi nyonga zilipo sikutiso andivuta🤷
Komabe chifundo changa chinaluza kwa aichochoyo😔
It was settled kuti mwanakazi akakhale pamwendo pa awowo.😢
As she was going kokakhala pamwendo pa oipayo ine Tha! Tha! mnaxakumbukila nthumba ndili ka change🤨 ndangoti.
"Ah amayi basi mwanayo akhale pampando pali ka change penapake ndimulipilira🥱",apano mtima unaphwa kuti l have helped a sister in need😌
Koma matsinya waonesa aichochowo eeh chifundo chinaphesadi nkhwali😛🙆
Nde anandithokozatu eeh😯 l can't forget how l felt when the girl was personally thanking me😇🥰
By the way wakufuna kwabwino andiojezeleko 7 hax transport yandipelewera😭😭
Ndufunika kukwera minbus ina please anthu a mulungu😫🙏