ZOONA

ZOONA Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from ZOONA, Arts and entertainment, Lilongwe.

29/04/2023

Komaso iye Lawi ndi Dr Namadingo akuzikayikira chani pa okha
Mpaka kukaitana kamzi gogo kaja
Ona kawadyeraso ndalama😂😂🙌
Komaso iwe AWIAWILO LONGOMBANAWILO LONGOMBAkuluza uwo

09/04/2023

Achina Gattah Ase tikudikira hip hop yina
Fact up tayiloweza😁

09/04/2023

Ku Zoona kuno timafira Fredokiss

09/04/2023

Sikulina Gwamba naye azatopa ndikubweza ma beef ose a Waxy Kay pakamozi

10/01/2023

Same Cris ya cholera ija mwaichita zithu🔥

08/01/2023

Interviewer: How much amount of milk does
your cow produce?
Farmer: which one, black one or white one?
Interviewer: Black one
Farmer: 2 litres per day.
Interviewer: And the white one?
Farmer: 2 litres per day.
Interviewer : Where do they sleep?
Farmer: The Black one or the. White one?
Interviewer: The black one
Farmer : In the Barn
Interviewer: And the White one?
Farmer: In the Barn also
Interviewer: Your cows look healthy... What do
you feed them?
Farmer: which one..black one or white one?
Interviewer: Black one
Farmer: Grass
Interviewer: And the white one?
Farmer: Grass
Interviewer: (Annoyed) but why do you keep on
asking if black one or white one when answers
are just the same??
Farmer: Because the black one is mine.
Interviewer: And the white one?
Farmer: Its also mine.

Alimi akwanyezelera ku Phalombe 😂😂

07/01/2023

Komaso FREDOKISS ma barz ena ama lowa off

ACHIFWAMBA AVUTA!_ Comedian avulazidwa ndi achifwamba ku Mzuzu.Ligo B Ligomeka ndi comedian odziwika bwino amene amakhal...
22/10/2022

ACHIFWAMBA AVUTA!
_ Comedian avulazidwa ndi achifwamba ku Mzuzu.

Ligo B Ligomeka ndi comedian odziwika bwino amene amakhala Ku Mzuzu.
Ambiri timamudziwa nditima short clip comedy tomwe amapanga ndi mzake otchedwa Emtee mw.

Panthawi yomwe amachoka town ya Mzuzu anatsikira chakufupi ndi Police, atangotsika, ndikutenga shortcut , anangozindikira achifwamba akubwera kwaiye alipanjinga za moto atanyamura zikwanje ndi ma chain.

Achifwambawo anavala ma mask nkumamufunsa kuti akupita kuti, kenako ndikumumenya ndi chitsuro kangapo kunkhope.

Anamusiya atakomoka ndipo anthu odutsa anamupeza patadutsa kanthawi ali chikomokere, panalibe chomwe amakumbukira poyamba ndipo zinamutengera nthawi kuti akumbukire chomwe chidachitika.

Tikunena pano akulandila chithandizo kuchipatala.

(Sensitive picture)

21/10/2022

Onesmus ku channel O
Ngati mkuwonera TV turn channel O angoyika nyimbo za onesmus mosemu ayambira🔥🔥👋

21/10/2022

Bro l joined bet cuz l was broke
Now am poor 😒

21/10/2022

Gwamba ukapeza tawi umuyendereko Natasha uja ukati akusowa mtengo ogwira
Mwina kumuganiziramo

Komaso gogo nasibeko uja ngati she is still a live visit her too
Mwina Peter ndi mwayi sakumuganizirabe gogo uja
NABOLA KUSACHE being a real story

20/10/2022

Black Nina mwayambaso kuyera
Nde tizingokuchulani YERA NINA

19/10/2022

Hie Admin
Plz hide my ID
Muthune ndimakhala ndekha
Nde thawi zambiri kunyumba kwangaku kumakoda kubwera nzanga
Ndi chibwezi chake kuzadyana
Ndi nzanga singamukanire
Nde chandidabwisa lero mamawa ano kwabwera chibwezi Cha Nzangayo
Ati azandithandize kukolopa since amangogwirisa ntchito nyumba yanga osakhozamo
Koma zomwe akupanga zandidabwisa
Infact abwera ndizifukwa zake
Koma nzangayoso achokapo apita kumuzi kwawo kumaliro abwera Sunday

Nde Satana ineso ayamba kundizinga
I think satanayi andiyendera lero
Nde Nditani ine
Plz kwa inu muli pa line help me
Sindikufuna kuzayambana ndi zangayo ine

Guys khani iyi mkutipo chani
Chakudya chamamawa mwina atani?

16/10/2022

Hie zoona
Bohboh
Ndimvekeni chigoba
Ndine mnyamata wa zaka 21
Ndili form 3
Ndimakhala ku Lilongwe
Munthune ndinali ndi chibwezi
Tinapezana ku party ya nzanga mwezi wathawu pa 4 koma tikapangira ku Salima ku nyaja
Ndi kaziyo titacheza bwino ku salimako tinapasana ma number
Ndinamufusira sanavuteso andilola
Chibwezi chathu chikayenda bwino
Moti katundu ndinadyako katatu kose

Week yatha sunday
Kaziyo anandipasa ring ya silver
Ma ring odula aja ngati gift
Nde ine Friday zapezeka kuti ndasowesa Kaya ndinasowesa bwanji
Koma zomwe zinayamba kundionekera
usiku nditagona ndinalota ndili ndi sikanayo ku malo achilendo koma owopsa kwambiri
Sikanayo akundiuza kuti ring ili kuti
Ndinamuuza kuti ndasowesa anati ndimubwezeresepo apo bii
Ineso ndilowe nawo u satanic
Then anazasowa koma akawoneka olusa kwambiri
Nditazuka ndinapeza thupi langa thukuta lokha lokha
Mamawa sinachedwe koma kumuyimbira phone
Koma sanandipaseso komwe moni anangofikira poti wapangazo zandibowa ndikudula phone mpaka pano sakunyakhaso
Phone yake ndiyozima
Nditamufusa zanga uja anati kaziyo sakukuziwa anangobwera nawo ku party yakeyo since inali yolipilisa

Moti daily ndimalota akumandigona
Mamawa ndikazula shaft yanga ikumamwawa komaso imakhala yoyima mwina 1hours koma ndikumva ululu

Please athu Inu ndithandizeni nditani
Ndikuwopa kuwauza makolo anga
Komaso kupita kukapephereredwa
Mwina atha kundipha
Nditani ine

Mmmm guys Help him khani ndiyoopya iyi

16/10/2022

Hie Mr Zii
HIDE MY ID
Am a man age 24
Ndimakhala ku Mzuzu ku Chiputula
Ndimapanga business yogulisa zovala mtown
Zimandiyendera Saname
Ndinayamba nditango siya school form 4 after nditakhoza ma points opoyira
Koma ngakhale zinali chochi sinafune ku giver ndi moyo wanga
Ndapangapo ma business ambiri koma inagira msewu ndi imeneyi

Mu business yanga yomweyi ndinapeza kazi waku Luwinga
Timakondana kwambri
Amabwera kunyumba kundiphikira ndikumabweresa chakudya kumsika ndikumadyera limozi
Potiso kazi ameneyi kwao kunali koyiphula
Kotero ndiwo ndi ma grocery ena amangula ndi iyeyo
Moti Zinafika poti chikondi chimachita kusekemera mthupi langa lose
Chikondi samababisa ndipo zikuchita kuonesa kuti sandizemberaso

Koma chasitsa zaye kuti Njobvu ithyoke nyanga ndichoti sikanayi akhala akugonedwa ndi bambo ake omubereka since Ali ndi zaka 12 pano Ali ndi zaka 20
Akuti bambo akeyu anasiza zimenezi mwanayi atafika zaka 18
Sindikuziwa kuti ndichizimba or chani

Khaniyi anandilongosolera ndi wina wake anandiona ndi sikanyi
Otiso sindikumuziwa komwe
Koma nditafusa chibwezi changacho sichina kane chinavomera koma ananena kuti sikunali kufuna kwake koma anamuyamba alimwana anali asakuziwa komwe kuti chikuchitika ndichani, cholakwika or ai until anangozolowera

Nde ndimapephako ma ganizo kwa athu anu kuti nditani
Ndingothesa chibwezi chathuchi
Mwina tizingopitilira cuz apa ndangobalalika or ku msika Sindikupitaso

Guys help him ine zandikukira💔

17/09/2022

Koma titulusireni Fredokiss tikufuna timenye naye Khondo yomutulusa MUSSAH 🙅

Send a message to learn more

23/08/2022

Follow this page imene izikupasirani khani zokhazo zoona za mdziko lathu la MALAWI

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when ZOONA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share